Malawi 24/7

Malawi 24/7 A better malawi for all it's possible.... Talking about politics and other news across the world

13/09/2025

Tiyen tikachose MCP pampando inu

walero fire fire
09/04/2025

walero fire fire

14/03/2025

Awa asazivute... Prophet Bushiri is going no where!!!

We rise together and fight for the son of the soil...

25/02/2025

Please invite a friend to follow us

25/02/2025

Ukutu kwanukha uku

Aluza bwanji awa
23/01/2025

Aluza bwanji awa

30/10/2024

Malawi 24/7

Omeneyera ufulu anthu Sylvester Namiwa watula pansi udindo ngati membala wa komishoni yomwe inasankhidwa kuti ichite kafukufuku wa ngozi ya ndege yomwe inapha a Saulos Chilima ndi ena.

A Namiwa ati achita izi chifukwa komishoniyi ikukana kuchita kafukufukuyu poyela ndipo iwo sakufuna kukhala nawo mbali yochita zinthu mobisa.

A Namiwa, ati akanakonda kafukufukuyo akanamonetsedwa pa kanema ngati momwe akubanja anapemphera ndipo nzomvetsa chisoni kuti komishoniyi yakana izi.

Iwo alembera kalata ofesi ya mtsogoleri wa dziko lino komanso komishoniyi kuwadziwitsa za chiganizo chawo

Wolemba: Ntola nkhan wathu...

Or muli inu mukadatan!!!??
30/10/2024

Or muli inu mukadatan!!!??

Maranatha! Kwangosala masabata atatu kuti mpingo wa Bangwe SDA Church awuchotse mundandanda wa mipingo ya SDA.
30/10/2024

Maranatha! Kwangosala masabata atatu kuti mpingo wa Bangwe SDA Church awuchotse mundandanda wa mipingo ya SDA.

26/10/2024

MULI MBALI ITI ? ⚽️
3pm⏰️ Tnm Super League :- Noma vs Bullets
9pm ⏰ La Liga:- ️ Real Madrid vs Barcelona

Happy birthday amuna awo a amathu..... Langizo... Mkazi uja mwachoka naye kutali ndiopilila enawo akungofuna amalizise k...
26/10/2024

Happy birthday amuna awo a amathu..... Langizo... Mkazi uja mwachoka naye kutali ndiopilila enawo akungofuna amalizise ka 1 mita kaja

WHAT I find difficult to understand about gaay marriage is that one of the couples dresses like a man while the other, l...
26/10/2024

WHAT I find difficult to understand about gaay marriage is that one of the couples dresses like a man while the other, like a woman.

Since it's a man marrying a man or a woman marrying another woman, why don't both couples dress as men or as women as the case may be?

There is something fundamentally wrong with gaay relationship and marriage.

By one partner dressing as a groom and the other as a bride, it means they believe that marriage is supposed to be between a man and a woman...

Address

Kenneth Kaunda Street
Manasi

Telephone

+265996155015

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Malawi 24/7 posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Malawi 24/7:

  • Want your business to be the top-listed Business in Manasi?

Share