Afro Tunes Malawi

Afro Tunes Malawi Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Afro Tunes Malawi, Blantyre.

BREAKING NEWS Apolisi abalalitsa anthu omwe amafuna kuyamba kuchita zionetsero pa bwalo la Lilongwe Community pomwe aphu...
25/11/2024

BREAKING NEWS

Apolisi abalalitsa anthu omwe amafuna kuyamba kuchita zionetsero pa bwalo la Lilongwe Community pomwe aphulitsa utsi okhetsa misozi.

How Females without academic qualifications take photos. 😂
25/11/2024

How Females without academic qualifications take photos. 😂

25/11/2024

A police ku lilongwe aponya teargas kwa anthu omwe anasonkhana pa lilongwe community ground kuti apange ma demo lero.

Ma demo a lero ndi achilendotu zikuchitikadi izizi?
25/11/2024

Ma demo a lero ndi achilendotu zikuchitikadi izizi?

See the top 10 pictures of GWAMBA holding his iPhone 👇
25/11/2024

See the top 10 pictures of GWAMBA holding his iPhone 👇

 Bungwe la Shepherd Bushiri Foundation ndi katswiri ochita zisudzo zapakanema (mafilimu) waku Nigeria uja adachitsa kale...
26/02/2024


Bungwe la Shepherd Bushiri Foundation ndi katswiri ochita zisudzo zapakanema (mafilimu) waku Nigeria uja adachitsa kale lathu kukhala lokoma ndi mafilimu aku Nigeria Nkem Owoh kapena kuti Ukwa asayinilana mgwirizano omwe cholinga chake ndikutukula mafilimu amdziko lino.

Malingana ndi kalata yomwe bungweli latulutsa lero, ubalewu sudachitikeposo mumbiri yamafilimu mdziko lino, kuti ochita mafilimu amdziko lino azigwira ntchito limodzi mdi aku Nigeria.

Moti tunena pano, pali filimu yomwe ikubwera yomwe ochita mafilimu aku Malawi ndi aku Nigeria achitile limodzi kuyambira mwezi wa April.

Posachedwa bungwe la Shepherd Bushiri Foundation litulutsa kalata kuti aluso lochita mafilimu mdziko lino alembere momwe angapeze nawo mwayi ochita nawo filimu ndi akatswiri aku Nigeria.

(by Dope kid -Blantyre:02/26/24)

Mutale Mwanza Shingles is early sign of  HIV/AIDS  are you ready to start ARV ?😂.🙆‍♂️😭💔
15/02/2024

Mutale Mwanza Shingles is early sign of HIV/AIDS are you ready to start ARV ?😂.🙆‍♂️😭💔

Dev Mak Artist naye amafika potopa mpaka wang'alula fan wake kuswa kuswa zilikotu ziliko mhu😂
12/01/2024

Dev Mak Artist naye amafika potopa mpaka wang'alula fan wake kuswa kuswa zilikotu ziliko mhu😂

03/01/2024

Bwana Malinga Mafia munasiya kuponya ma ticket a bet? January tu uyu tamaponyani tizipeza ya ufa😂

10/12/2023

Next year replacement ya Zeze azakhala FADA 😂

Take screenshot.

Address

Blantyre

Telephone

+265998351348

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Afro Tunes Malawi posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share