UNCLE NOAH

UNCLE NOAH Hardware and general supply

15,000
07/01/2026

15,000

Leopard cutting disc 80000
03/12/2025

Leopard cutting disc 80000

Timakhala ndi paint ntundu uliwonse pa mitengo yovelela
03/12/2025

Timakhala ndi paint ntundu uliwonse pa mitengo yovelela

03/12/2025
Red oxide available
02/12/2025

Red oxide available

150,000
01/12/2025

150,000

25/09/2025
Pomwe kafukufuku ali mkati pofuna kupeza dzingawenga dzomwe dzapha a Victor Anthony m'banda kucha wa lero m'boma la Dedz...
07/09/2025

Pomwe kafukufuku ali mkati pofuna kupeza dzingawenga dzomwe dzapha a Victor Anthony m'banda kucha wa lero m'boma la Dedza, zadziwika kuti dzingawengazi zinakonza bowo pa mpanda pomwe anagwiritsa ntchito polowa ku malo komwe malemuwa amakhala.

Atalowa mkati, anakwanitsa kumanga mlonda kenako mkulowa kuchipinda komwe malemuwa amagona pogwiritsa ntchito zenera la kuchipindaku.

Atalowa, anayamba kuuza malemuwa kuti akufuna ndalama asanayambe kuwamenya ndi zitsulo komanso zikwanje kufikira atakomoka.

Kenako, zigawengazi zinayamba kufufuza zinthu mozungulira m'nyumba mwa malemuwa ndipo zaba ndalama zomwe padakali pano sizikudziwika kuti ndi zingati koma zinali ma Dollar, Lands komanso zina m'makwacha ndi p***a mfuti.

Address

P. O BoX 65
Blantyre

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when UNCLE NOAH posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share