KBS Group Malawi

KBS Group Malawi Your Ultimate Business Partner!

07/05/2026

I would like to thank each and every individual, institution, groups and organisations that wish me well on my birthday. I will always live to remember 7th May, 2026 because of you

18/04/2026
3M Brand New TOSLINK /Optical CablePezani cable ya original ya optical yomwe m***a kugwiritsa ntchito pa Sound bar, TV, ...
18/04/2026

3M Brand New TOSLINK /Optical Cable

Pezani cable ya original ya optical yomwe m***a kugwiritsa ntchito pa Sound bar, TV, STB komanso ma player osiyanasiyana

MK 38, 500 yokha basi
Lilongwe
0888882830 l 0994890030

Available in Lilongwe now
18/04/2026

Available in Lilongwe now

Portable Key chain COB lightSuper brightMulti-mode, including SOSIt's shower proof and has a bottle opener. Type C charg...
02/04/2026

Portable Key chain COB light
Super bright
Multi-mode, including SOS
It's shower proof and has a bottle opener. Type C charging port and 100mAh LiPO battery

MK 10, 500
Lilongwe
0888882830 l 0994890030

OKOP Portable Sound Bar KP-557Get this state of the art sound bar that will amaze you with its crystal clear sound and i...
02/04/2026

OKOP Portable Sound Bar KP-557
Get this state of the art sound bar that will amaze you with its crystal clear sound and incredible bass yet affordable MK 78, 500 only for this 20W R. M. S. punch

It packed with TWS, USB, TF Card Slot, FM Radio, Bluetooth, AUX and RGB

Lilongwe
0888882830 l 0994890030

Pomwe moyo wathu ukudutsa mu zithu zosiyanasiyana, zabwino komanso zoipa ndi zowawa timafunika chilimbikitsoKaya ndi bus...
25/03/2026

Pomwe moyo wathu ukudutsa mu zithu zosiyanasiyana, zabwino komanso zoipa ndi zowawa timafunika chilimbikitso

Kaya ndi business komanso chili onse chimakoma moyo wa uzimu ukakhala olimba

Pezani Audio Bible pa mtengo ozizira wa MK 30, 500 yokha basi pa order kapena MK 50, 500 bible limodzi lokha.

Mumapanga charge, ndilosabvuta kugwiritsa ntchito komanso muli zilankhulo zingapo kumpatikizapo chichewa

Chaka chino amzanu komanso abale ndi makolo tawaguliraniko mphatso yosaiwalika, eya inde inu Bible. Cake adya koma amaiwala koma bible simudzaiphonya

Lilongwe & Kasungu
0888882830 l 0994890030
https://www.facebook.com/share/1DBWcXnsDs/

Mukapita ku shopping lero kapena tsiku lina lilironse chonde musakaiwale kugulako katundu wa 4TEE Foods ProductsKaya ndi...
25/03/2026

Mukapita ku shopping lero kapena tsiku lina lilironse chonde musakaiwale kugulako katundu wa 4TEE Foods Products

Kaya ndi White Vinegar, Piripiri kapena Kambuzi Sauce, iwowa ali naye ndipo amamupanga moyelekeza nokhumba zanu komanso mwapamwamba zedi

Koma ngati muli ndi mpata tiyeni tikangokumana ku Trade Fair

Pankhomo komanso inu a business ya zakudya tapezani tsabola ndi vinegar wa 4TEE mudzanditsimikizira ma customer mutayamba kuwalemphera kamba ka kukoma kwa zakudya zanu

Address

Limbe
Blantyre
P.O.BOX5715,LIMBE

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when KBS Group Malawi posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share