31/08/2026
Kodi mukufuna wall portrait? Kapena muli ndi anzanu kapena abale omwe mukufuna kuwapangira?
Ife timapanga ma wall portrait a Canvas komanso a Glass okongola kwambiri, apamwamba, komanso pa mtengo wabwino.
Mitengo Yama Potrait :
CANVAS ( BANNER MATERIAL):
• A0 (84 × 118 cm) – MK65,000
• A1 (59 × 84 cm) – MK45,000
• A2 (42 × 59 cm) – MK30,000
• A3 (29 × 42 cm) – MK20,000
• A4 (21 × 29 cm) – MK15,000
GLASS PICTURE FRAMES PRICES :
• A3 — MK50,000
• A2 — MK80,000
• A1 — MK120,000
Free delivery around Blantyre.
Timatumizanso kulikonse Malawi muno kudzera pa CTS,Speed,Post office or Direct minbus.
Contact us or WhatsApp: 0994 93 66 00