25/05/2026
UPDATE πβοΈ ON π§
`LIMPOPO FM NEWS π²πΌ π»ποΈπ°ππ»π₯πΆπππ°πβοΈβ‘π³οΈπΊππ
ππ`π``
*π²πΌπ°FM NEWS UPDATE ON LIMPOPO π° π²πΌ*π₯π₯π₯
*MNBINA π βοΈπ§π§*
β
βKhonsolo ya boma la Mangochi yalengeza za imfa ya mfumu yaikulu (TA) Mkata ya bomali.
β
βMalingana ndi khonsoloyi, TA Mkata yomwe inali pansi pa Senior Chief Jalasi, yamwalira dzulo pa chipatala cha Mangochi pomwe anayigoneka, itadwala kanthawi kochepa.
β
βKhonsoloyi yati mfumuyi anayigoneka pachipatalachi Lachisanu. Mwambo woyika m'manda malemuwa uchitika lero m'mudzi mwa Mkata.
β
β *BY MNBINA πβοΈ FM NEWS UPDATE*