Find your partner

  • Home
  • Find your partner

Find your partner Takulandini pano pa page ya find ur partner. send details 0745046120

Wadya ZaulereMtsikana mukumuona yu wathawa kupita kwa mwamuna wina kusiya yemwe adamuitanitsa kumudzi.Nkhani yi ik*ti mu...
10/12/2025

Wadya Zaulere

Mtsikana mukumuona yu wathawa kupita kwa mwamuna wina kusiya yemwe adamuitanitsa kumudzi.

Nkhani yi ik*ti munthuyu adajoina Facebook. Ali pomwepa adapalana ubwenzi ndi mwamuna yemwe Ali ku South Africa.

Poti mudziwa anyamata ambiri omwe ali ku South Africa ngamdede akaona mkazi wokongola pa Facebook basi tu anthu wa adalimbitsana k*ti atsatilane.

Dongosolo lonse mwamuna yo adachita. Adamukonzetsela mkaziyu passport ndi k*tumiza so ndalama ya transport.

Pamene amachita izi mkaziyu amalumikizananso ndi chibwenzi chake chomwe chili ku South Africa ko.

Tsiku lonyamuka litafika munthuyu adauyamba kupita ku Theba k*ti alowe moyo womadyera nsima ndiwo mazira masana madzulo ngati ayao.

Atafika ku Theba ko mmalo momuimbila yemwe amukonzetsela passport adangothima foni nkuitana uyo chibwenzi chake k*ti akamutenge.

Atafika uko uja adamuchitila zonse akaimba akumamuuza asamuimbilenso iye ngokwatidwa akafuna apite kumudzi akapeze mkazi wake.

Tikunena pano mnyamata yemwe adatumiza ndalama yi akungokhalila mamina loliloli kulira R6000 yake yomwe aononga pa mkazi uyu.

AK*TI ANALIPIRA MZIBAMBO YEMWE ANAKUMANA NAYE ONLINE K*T AMUZUNZE NDKUMUPHA So mtsikana mukumuona pachithunziyu dzina la...
10/12/2025

AK*TI ANALIPIRA MZIBAMBO YEMWE ANAKUMANA NAYE ONLINE K*T AMUZUNZE NDKUMUPHA

So mtsikana mukumuona pachithunziyu dzina lake nd sonia exelby wazaka 32 ochokera ku US anapezeka atafa ku frolida after atakumana ndi mzibambo mukumuona pachithunziyu Dwayn hall wazaka 53.

Ak*ti Sonia anapanga post pa website ina yake k*t akusaka munthu oti adzampange kidnapp kenaka akamzunze ndkumupha,then dwayn hall anamuyankha sonia k*t iyeyo ndiokonzekq k*tero,sonia anakakwer ndege kupita ku frolida pa 10 October 2025 kumulondola HALL then hall uja anapita kukamutenga.

umbon unaoneka mufon ya sonia pamene hall amamuzunza sonia nkumupha,apolisi anapeza thup lasonia lili kwala pamalo ena ake ku frolida ko .

HALL WAGAMULIDWA KUKAKHALA KUNDENDE MOYO WAKE ONSE,😁🙌💔

Kumbali ya amuna izi mumaona k*ti zili mphindu lotani?
09/12/2025

Kumbali ya amuna izi mumaona k*ti zili mphindu lotani?

onerani mfana uja mmene wagayira aphunzitsi akefull video mu comment section 👇👇
05/12/2025

onerani mfana uja mmene wagayira aphunzitsi ake
full video mu comment section 👇👇

Mfana uyu wangochepa koma atha ntchito Ndi dolo
05/12/2025

Mfana uyu wangochepa koma atha ntchito
Ndi dolo

sad news 💔Mtsikana uyu yemwe dzina lake ndi Beatrice wapezeka atafa ku Area 49 kuseli kwa sukulu ya Pulayimale ya New Sh...
29/11/2025

sad news 💔

Mtsikana uyu yemwe dzina lake ndi Beatrice wapezeka atafa ku Area 49 kuseli kwa sukulu ya Pulayimale ya New Shire atamubayabaya komaso ali maliseche, zikumvekaso k*ti wasiya mwana wang'ono.
rest in peace

aja amagwira ku mayfair aja akanabwera kuzasesa azimayi omwe akuchita nyasi mchinyumba ichi kusiyana ndi aja omwe awaten...
20/11/2025

aja amagwira ku mayfair aja akanabwera kuzasesa azimayi omwe akuchita nyasi mchinyumba ichi kusiyana ndi aja omwe awatenga angwiro aja oti amazilimbikira mwaiwo okha

20/11/2025

Today in joz

Address

Area 7

2030

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Find your partner posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

  • Want your business to be the top-listed Business?

Share