Mzanga TV

Mzanga TV 🇲🇼🌍
(4)

23/05/2025

Komatu Landlord amacheza bwino ndi a tenant akewa🤣

23/05/2025

Kungozolowera kunamizidwa basitu🤣🤣🤣

Collabo iyiyi osayiphwekesa!Praise Umali and Theresa Phondo
23/05/2025

Collabo iyiyi osayiphwekesa!

Praise Umali and Theresa Phondo

Ma Celeb tu ku Malawi kuno akusamukakotu🔥🔥🔥🔥
23/05/2025

Ma Celeb tu ku Malawi kuno akusamukakotu
🔥🔥🔥🔥

19/05/2025

Waxy uja amadyera udobadoba omwewu 🤣🤣🤣

19/05/2025

Good News atumiki. Ifetu dzikoli tikonza tokha. Andalewa akutiyesa kwambiri

Munthuyu moyo wake uli TuliChifukwa ndiye wawubisa moyo ndi wa mmwambayo Kapena mwamuwonako ku Nthunzi wa Chileka?🤣
19/05/2025

Munthuyu moyo wake uli Tuli
Chifukwa ndiye wawubisa moyo ndi wa mmwambayo

Kapena mwamuwonako ku Nthunzi wa Chileka?🤣

Ubongo wa ELI Njuchi ma size ake ndi achina Mkasa, Billy Kaunda, Lucious Banda, Mlaka Maliro… Mwanayu Anabadwa mochedwa ...
16/05/2025

Ubongo wa ELI Njuchi ma size ake ndi achina Mkasa, Billy Kaunda, Lucious Banda, Mlaka Maliro… Mwanayu Anabadwa mochedwa koma bwenzi atayimba nawo Reggae ya Balaka…

Kamvereni album ya Cifu ngati ndikunama… tabetcha 5 sauzande

15/05/2025

Ndiye kuti a p**e kugwetsa kwacha kuja anangotaya nthawi yawo?

Kuyendesa dziko di ndi ntchito yofunika luso lapadela

A Minister Vera Kamtukule atchenatu🥳🥳🥳🥳
15/05/2025

A Minister Vera Kamtukule atchenatu🥳🥳🥳🥳

A Zonke Too Fresh aja ndi a ma move a smooth!🤣🥳
15/05/2025

A Zonke Too Fresh aja ndi a ma move a smooth!🤣🥳

14/05/2025

Dzulo mnakalowa rent nyumba ya tsopano. Vuto langa ndiloti ndayiwala kuti nsewu wake ndi uti…

Ku Ndirande kuno zimatele?😔

Address

40005
Lilongwe

Telephone

+265881284955

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Mzanga TV posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share