Choyamba, Tidye

Choyamba, Tidye Quality foods for a hunger-free Malawi. Together, we fight hunger, malnutrition, and food shortages by providing quality food products β€” for a healthier Malawi.
(1)

Our Malawi, Our pride.

01/05/2026

Mpunga wa TC11 komanso ufa, zikupezeka pa mtengo wabwino!

Tiyimbireni pa 0999232901


γ‚š

Anzanu achangu zikuwayendera ndipo akuchitira umboni!Gulani kapena kuyitanitsa wanu Ufa kapena Mpunga pa nambala iyi πŸ‘‡0 ...
29/04/2026

Anzanu achangu zikuwayendera ndipo akuchitira umboni!

Gulani kapena kuyitanitsa wanu Ufa kapena Mpunga pa nambala iyi πŸ‘‡

0 999 232 901


γ‚š

25/04/2026

Kwacha koma choyamba tidye!

Mpunga wa Kilombero, mma pack a 5kg ndi 2kg

Ufa wa gaiwa, gramil ndi oyera wama vitamins ndima Minerals mma pack a
5kg ndi 2kg

Chimanga cha Popcorn pack ya 500g

For orders and delivery:
Call on:
+265 999 23 29 01

fans

γ‚š

09/03/2026

Kwacha koma choyamba tidye!

Mpunga wa Kilombero, mtengo ndi:
5kg - k30,000
2kg - k12,000

Ufa wa gaiwa, gramil ndi oyera wama vitamins ndima Minerals uliponso.

Mtengo:
5kg k10,500
2kg k4,500

Chimanga Popcorn, mtengo ndi:
500g - k4,000

For orders and delivery:
Call on:
+265 999 23 29 01


γ‚š

02/03/2026

Mpunga okoma wa TC 11 Kilombero ukupezeka.

Tiyimbireni pa 0999232901



Kodi munaulawa mpunga wa TC11 Kilombero?Tatiuzeni ndemanga yanu mu vomment section?   γ‚š
16/02/2026

Kodi munaulawa mpunga wa TC11 Kilombero?

Tatiuzeni ndemanga yanu mu vomment section?


γ‚š

Kuli masewera atsikana achitanyu pa Bingu Stadium masanawa pakati pa Malawi U-20 ndi Guinea BissauMpirawu ndiwa ulele ko...
14/02/2026

Kuli masewera atsikana achitanyu pa Bingu Stadium masanawa pakati pa Malawi U-20 ndi Guinea Bissau
Mpirawu ndiwa ulele koma nkutheka mufuna
Popcorn
Mpunga
Ufa
Apa mwayandikira kuchimake kopezeka katunduyu wa TC 11

Tiyankhuleni pa 0 999 232 901


γ‚š

Ndika mvula kameneka popcorn angakometu kumwera chai β˜•οΈπŸΏ500g ali pa k4,000 yokha basi.Tiyankhuleni pa 0999 232 901   γ‚š
13/02/2026

Ndika mvula kameneka popcorn angakometu kumwera chai β˜•οΈπŸΏ

500g ali pa k4,000 yokha basi.

Tiyankhuleni pa 0999 232 901


γ‚š

Awatu adya!Alipo samafuna kudya?Ndi k12,000 (2kg) kapena k30,000 (5kg) m***a kupeza wanu.Tiyimbireni pa nambala iyi πŸ‘‡0 9...
13/02/2026

Awatu adya!
Alipo samafuna kudya?

Ndi k12,000 (2kg) kapena k30,000 (5kg) m***a kupeza wanu.

Tiyimbireni pa nambala iyi πŸ‘‡

0 999 232 901


γ‚š

Address

Mzuzu
GULLIVERAREA49

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Choyamba, Tidye posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share