24/03/2026
Pamene mvura ya mphamvu ikupitilira kugwa mdziko muno, tikhare atcheru ndi osamala.
Chithunzichi chikuzungulira mmatsamba a mchezo ndi chimodzi mwazinthu zomwe zitha kupangitsa kuti tiludze miyoyo yathu . Mapolo amagetsi agwa ambiri mmadera ena mpaka madera ena misewu ikutsekedwa. Chonde tikhare osamala tikamadusa malo oti kwagwa mapolo amagetsi. Zomwe wachita mayi wathuyi sizabwino. Nyesi imapha. Kharani osamala.
Timakunyadirani ma followers athu😊.
Photo: Social media