20/01/2016
Labour Relations Resolution consult imathandiza anthu onse ogwira ntchito mma shops,mma nyumba ndi mma company mu zinthu izi:kukukambirani mulandu akakuchotsani ntchito,kuwerengetsa ndalama zanu zonse pa nthawi yonse yomwe mwakhalira pa ntchito, kukulemberani kalata yosiira ntchito,kukuimirirani pa mulandu wanu ku khothi,kukupezerani ntchito,kupezera mabwana anthu a ntchito,kuthetsa nkhanza pa ntchito,kukuthandizani kuti malipiro akwere pa ntchito.mukafuna kudziwa zambiri kapena thandizo lankhulani ndi Frank Dulli pa nambala iyi:0885556831.LRRC liwu la anthu ogwira ntchito(the voice of workersa).