12/10/2025
Register today!π₯π₯π₯π₯
Pamene Mwambo wa Beauty Fan Fair wayandikila kuti uchitike pa Bwalo la Masewero la Bingu pa 1 - 2 November 2025, ELK Management ikukumbutsa Mavenda nonse kuti m***a kulembetsa ndi cholinga choti mukaonetse ndikugulitsa Malonda anu ku Mwambowu.
Kukembetseku kutsekedwa pa 20 October 2025.
Uwu ndi Mwambo omwe ukabweletse pamodzi ma Nail Technicians,Gym owners, Makeup Artists, Onse ochita za Salon, Fashion designers, Ogulitsa mawig, Eni ma Restaurant ndi ena onse omwe amapanga malonda okhuza kukongoletsa khungu.
Mwazina kumenekuso kukapelekedwa Mendulo kwa Akatswiri m'magawo osiyana polemekeza ntchito yawo yotamandika yomwe akugwila m'dziko muno.
Kuti mumve zambili imbani kapena WhatsApp ma number omwe alimmusiwa
0884 63 96 78
0884 41 62 47