17/11/2025
Hi Admin, ndine mkazi wa zaka 30 ndili kuno ku Kempton park. ndikufuna mamuna wa chibwenzi tidzakwatirane mtsogolomu, akhale wa mbali ya konkuno ku Kempton park, ndili ndi mwana mmodzi ali kumudzi ku Malawi, mamuna osaposera zaka 36 wamaonekedwe abwino.