22/12/2025
LAND VALUE ASSESSMENT
Kodi mukudziwa kuti Malo ndi chithu chomwe tiyenera kusamalisa tikafuna kugura???
Malo amagulidwa pa Mitengo yosiyana siyana malingana ndi value yamalo makamaka omwe tufuna kumangapo timaona location yomwe malowa ali. Aku 43 amadula kuposa Aku Lumbazi
So tatiyeni tione pomwe tufuna kugula Malo olimapo, timakanika kuziwa Kae value ya Malo anthu omwe tufuna kugura kuti tizilimapo ndipo timangogura Malo aja. koma mukuziwa kuti izizi ndi Risk payokha???
Mwachoncho tikafuna kugura kapenà kugulitsa Munda, tiziyamba taona value yake ya Mundawo pambali pa kukula kwake. Tiyeni tione ngati Mundawo ULI ndi chonde kapenà ai ndipo ndalama zifanane ndi chonde chamundawo.
Izizi zizatithandizira Ku saver ma cost omwe atha kulowa pa kugurà zipangizo za Ulimi zolowa pa mundapa.
Ife akadaulo aza Donthi titha kukuthandiza kuziwa value ya Malo anu ndipo tipezeni ife thawi yomwe mufuna kugulitsa kapenà kugurà Malo anu ndipo ife tizakupangirani Survey mwa ka mtengo ka ziiiii