03/09/2026
ALIMI A KU SOUTHERN REGION, NTHAWI YANU YAKWANA!
Kuyambira m’minda yaing’ono mpaka kuma farm akuluakulu, Khoza Investments ili nanu paulendo wokulitsa ulimi.
Tikubweretsa ma tractor, ma implements ndi makina a ulimi osiyanasiyana othandiza kuti ntchito ya m’munda ikhale yosavuta, yachangu komanso yopindulitsa.
Kwa alimi onse ku Southern Region pitirizani kulima, pitirizani kukula, chifukwa inu ndi amene mukudyetsa Malawi!
Tiyimbileni pa: 0992808855 kapena 0882808854 kuti munve zambiri.
KHOZA INVESTMENTS! BWENZI LANU PA ULIMI WAMAKONO!