Malonda KU Katuli - about Businesses kwa ogula ndi ogulitsa malonda.

  • Home
  • Malawi
  • Mangochi
  • Malonda KU Katuli - about Businesses kwa ogula ndi ogulitsa malonda.

Malonda KU Katuli - about Businesses kwa ogula ndi ogulitsa malonda. Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Malonda KU Katuli - about Businesses kwa ogula ndi ogulitsa malonda., Business service, C/O MDINDE PRIMARY SCHOOL P. O BOX 14 KATULI, Mangochi.
(1)

13/05/2025

Musavutike kufuna kufuna kogula mbewu monga chimanga komanso soya ndi nyemba.Kaguleni kwa aKatuli kalanje near Mozambiquean border...

18/10/2020

Malo otchipa okwana kumanga nyumba imodzi ndi ma boys quarters awiri ogulitsa kwa uluche near ndendeuli, (Katuli trading center) tengeraniko mpata okhala ndi Malo otchipa chonchi wa pa mtengo wa K250 000 negotiable. Wap +265885679932...

Muli ku Joburg ndipo mukufuna kutumizira ndalama anthu kumudzi komano mtengo wabwino osinthira ndalama zanu siukupezeka?...
17/09/2020

Muli ku Joburg ndipo mukufuna kutumizira ndalama anthu kumudzi komano mtengo wabwino osinthira ndalama zanu siukupezeka? Don't panic chifukwa yankho lanu lafika ndi Matata cash express.... Kupeza ndalama zanu muli chikhalire pa khomo panu. Chonde yimbani pa ma nambala amenewo kuti mulumikizane nawo.

13/04/2020

Shop for sale pa Katuli trading center, call or wap pa +265885679932

09/04/2020
09/04/2020

Covid19 jisawisyedi, amtamose nganijiyiche kumangwetu kuche Katuli kuno chonde kwende tulisamale pakuya malamusi gakutusalila wa chipatala.Pakuchapa mmyala ndayi syose, kutalikangana katame, ngapelegana makono chisawawa nikutendela mwisamulo pa mbindi pa mkono...

Almost new, inagudwa last month ndipo mwini wake akufuna 500k last basi... +265885679932 Wap...
08/12/2019

Almost new, inagudwa last month ndipo mwini wake akufuna 500k last basi... +265885679932 Wap...

For the top guys, and it's going at cheaper price. If interested come to inbox or wap +265885679932
07/11/2019

For the top guys, and it's going at cheaper price. If interested come to inbox or wap +265885679932

05/11/2018

GUYS CHONDE NGATI MULI NDI ZOGULITSA LENGEDZETSANI PA PAGE IYIYI CHONDE MOKUPHEMPHANI...

Address

C/O MDINDE PRIMARY SCHOOL P. O BOX 14 KATULI
Mangochi

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Malonda KU Katuli - about Businesses kwa ogula ndi ogulitsa malonda. posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share