The Great Mpondas

The Great Mpondas The best place to be in Mangochi

16/02/2024
22/05/2023

MPONDAS

16/10/2021

Mfumu Mswati ya Dziko la Eswathini, yati Anthu omwe akudana ndi ulamuliro wake ndipo akufuna ulamuliro wa Demokalase akhuta Chikokeyani ndikusuta fodya wamkulu wa Kanundu.

Mfumu Mswati wayankhula izi Ladzulori mu Mzinda wa Mbabane, M'dzikolo pa Mwambo omwe Iye amasekulira Chipatala cha Boma.

Mfumu Mswati inayankhula izi kamba ka Zionetsero zokwiya ndi ulamuliro wake zomwe zakhaka zikuchitika M'dzikolo pomwe ophunzira Sukulu akhala akunyanyala Maphunziro awo ndikuchita zionetsero Mzigawo zonse za Dzikolo.

Mfumuyi inapitilira kufotokoza kuti Anthu omwe akumatuntha Anthu kuchita zionetsero zodana ndi ulamuliro wake akumayamba alawa Ganyala pang'ono ndikukoka Ndudu ya fodya wa Kanundu akatero nkumafuna zokambirana ndi Boma lake.

Nzika za Dziko la Eswathini, Zikupitilira kuchita zionetsero zodana ndi ulamuliro wa chifumu ndipo zikunenetsa kuti tsopano yakwana nthawi yoti zikhale ndi Boma la Demokalase.

Ndine Grant Elisha Ngozo.

16/10/2021

Mu Mpondas ndi dela komwe ungapeze ntundu wa anthu ambiri, ndipo eni mudzi si anthu ozikonda ayi chikondi nde chikhalidwe chathu..

12/09/2021

KUNENA CHILUNGAMO TIKUTHOKOZA FANZ POPANGA LIKE PAGE YATHUYI MWAUNYINJI PITILIZANI KWAZIWITSA ENA..NDIPO ULEMU WANU

15/08/2020

Big up to for Putting Mpondas on the Map

New track Just Came out tittled
...

WhatsApp Me on This No 0619487097. To glab your copy.... It's Hot 💥💥💥

Address

Mponda

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when The Great Mpondas posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share