Peter kasimba Mwandira

Peter kasimba Mwandira FrequencyofGod

15/01/2022
15/01/2022
14/01/2022

HD Samsung Lens Camera.

Wi-Fi connecting with wireless YouTube, Facebook, internet

Battery ndimwalamwala
Phone 0884619067/0981852533.
4.5-22.5mm_____1:2.5-6.3__25mm.

Ndine Mnyamata wa Zaka 35 kwathu ndiku Hewe mu Boma la Rumphi.Munthune ndili ndi mkazi ndipo mkaziyu Ndimakukonda kwambi...
27/08/2021

Ndine Mnyamata wa Zaka 35 kwathu ndiku Hewe mu Boma la Rumphi.

Munthune ndili ndi mkazi ndipo mkaziyu Ndimakukonda kwambiri ndi mtima wanga onse.

Koma ndikutitu Koma..

Ndine munthu okonda mkazi wanga

Ndine munthu ofuna banja Langa lizikhala longalala nthawi zonse.

Ndine munthu olifunira zabwino banja Langa.

Ndipo Moyo wanga umakonda mtendere .

Ndimakhala oyetsetsa Kuti mnyumba mwanga mzikhala kuvetsetsana wina NDI mzake.

Ndipo ndine munthu wasangala nthawi zonse Koma kapezedwe kanga ndikopelewera.

Ndikakhumudwitsana ndimasakasaka njira yobwezeletsa umodzi mnyumba.

Koma Mkazi wanga nthawi Zina sandirakhula Bwino,Mpaka maganizo anga amafika Poti Bora kukhala Opanda mkazi,,,ndimakhala ndikuzifutsa mafutso Opanda mayankho,,,Kodi mkaziyu ndiwangadi kapena ndi wrong packing???? Kapena Sithiti Yanga?? Ndine munthu osausika Maka ndi Mau omwe ndimayankhulidwa ndi mkazi wanga,Chonde ndikufuna nthandizo lanu Kodi Nanu anuwo mkukhala Moyo Ngati wangawu kapena mkusangalala Kodi ndingatani???

Mayankho Anu ndi phudzuro Kwa iwe ndi ine dzikomo.

Address

Liwinga Mzuzu 2
Mzuzu

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Peter kasimba Mwandira posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share