Ntcheu-Escom-Branch

Ntcheu-Escom-Branch power all day evely day-malawi wide

16/12/2015

ntcheu yonse waliwali..........pakalipano

20/09/2015

black out ntcheu yonse

tikusinytha mapolo!

15/09/2015

Mphate things

23/08/2015

Ntcheu yonse waliwali...kwamene ali ndi mabulb.....

14/08/2015

Mukafuna kugula maunits a magetsi

mpamba
money

amenesangathe muthaso kugula pa ptc pa boma near total filling station..moyang anizana ndi bank yagulitsidwa ija msb

14/08/2015

Trip to mangochi

kalitera
dzinkambani
tiwana
chikulekule
madala
chiwanda


chisi


akwati

kapenuka on duty
12/08/2015

kapenuka on duty

ichocho man
12/08/2015

ichocho man

12/08/2015
10/08/2015

Tikukhulupila kute ntcheu yose ili mowala...kupatula amene alibe maunits...

Zikutheka

09/08/2015

Ntchito yochotsa nyani itha posachedwapa

Managment

09/08/2015

Tipeleke moni mmadela amene azungulira ntcheu

kumphate kwa eneya
gumbu,
mastemali,chinyamula,kandota,ben..
tsangano,ndagoma,
kasinje,.sela,kaloga,
ngalande,njolomole,mlangeni,dovico,
bwanje,nkhumba,
bawi stores,
nachitheme,
balakamarket..
pengapenga,
bwanje,birila,.
champiti

nditimadela tina tosaziwika ndi boma moni

magetsi ayaka nthawi iliyose nthimitsani zida zamoto tipewe ngozi

Address

Ntcheu
Ntcheu

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Ntcheu-Escom-Branch posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share