04/07/2022
Q.Kodi pogula malata ungadziwe bwanji kuti ndi 26, 28 or 32 "geji"?
A. Kusiyana kwama geji kwa end user atha kukudziwa poona thickness ya lata mukamalipinda
Komaso nthawi zambiri zimatengera kuti rim la malata amene mukugula ndi la quality yanji, izi mukhoza kuzidziwa pa mitengo ya malata imene mwa patsidwa and always look for AZ50