Talk it out with Dr. Patrick Bande

Talk it out with Dr. Patrick Bande Dr Bande is a Pan-African scholar and a free thinker from Malawi to the World. A social activist and China expert.
(3)

If you follow my page be prepared to see different perspectives to issues. I may question your beliefs, so be prepared for such moments.

Dzulo tapanga share post ya MBC yokamba za progress ya Jenda to Mzimba road.... Tikulimbikitsa boma lipitilize zimenezi....
09/09/2026

Dzulo tapanga share post ya MBC yokamba za progress ya Jenda to Mzimba road.... Tikulimbikitsa boma lipitilize zimenezi....komatu Kuma comment aliko anthu ochuluka onena kuti Izi ndi Za Chakwera.

Tithokoze a Chakwerawo pochita mbali yawo.
Ndiyesa a Mkulukuta Moyo nawonso muzawayamikira pa ntchito za M1 zomwe ayamba.

09/09/2026

Kwavuta.....
America ndi Iran akupitiliza kuchitilana za mtopola

08/09/2026

Asah, chimakhala chili chani?🥱🥱

Iyi idali 2025 July mmene ndidapita pa Fatima CDSS kukapeleka mphatso kwa ana amene adachita bwino pa JCE yawo. Panthawi...
08/09/2026

Iyi idali 2025 July mmene ndidapita pa Fatima CDSS kukapeleka mphatso kwa ana amene adachita bwino pa JCE yawo. Panthawiyi nkuti onsewa ali form 3. Ndipo ndidawalimbikitsa kuti ndikufuna pa form 4 tizamve ma points abwino.

Lero aphunzitsi anditumizila uthenga kuti highest wakhonza 13 points, ndipo alipo angapo amapointa abwino below 20.

Ayitu izi ndizokoma kumva, kukhonza bwino chonchi pa CDSS sizophweka. Ulemu wanu aphunzitsi nonse komanso ana amene achita bwino.

Amene mwalakwa osadandaula tiyeni tikaphunzire ntchito zamanja kumenekunso kuli tsogolo ndithu.

Keep doing this....don't stop
08/09/2026

Keep doing this....don't stop

08/09/2026

Bola pa jons basi, eti guys

Madolo osunga town.....Mwawadziwapo ndani apapa fans ya Blantyre
08/09/2026

Madolo osunga town.....Mwawadziwapo ndani apapa fans ya Blantyre

Wapadziwa.....Ulemu wanu biggie
08/09/2026

Wapadziwa.....Ulemu wanu biggie

08/09/2026

Captain .....

08/09/2026

Kwavutatu ku middle east

Address

23 Victory Close
Blantyre
DH87FB

Telephone

+265997406096

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Talk it out with Dr. Patrick Bande posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Talk it out with Dr. Patrick Bande:

Shortcuts

Share