05/08/2024
AKANAKHALA KUTI SIOYIMBA BWEZI ALI👇
1 Tuno :Ophika kachaso kwa Mayi Mbambande⚗️
2 Waxy Kay: Ogulisa mang'ina🍴
3 Charisma: Owotcha chimanga / dowe🌽
4 Onesimus: Owonesa video show📺
5 ELI Njuchi: Ometa mu mtandilemu✂️
6 Kell Kay: Yeloman okonza ma phone 📲
7 Gwamba: Wogaya munchigayo ku Ndilande
8 Toastt: Conductor wa Paseli🚍
9 QUEST MW: Nyamata wapa Pool 🎱
10 Mellz: Bush Dhi ogulisa zamba 🍃
11 Jay Jay Cee: Wakabanza anyamata anjinga za moto 🏍
12 6th :Uyuyu bwezi ali osegula ku mand⚰️
13 Wikise: Okumba zitsime ku 50, Kwa Cent, mwa Mgona ⛏️
14 Zeze :Telala wa kwa Jali♿
15 Chizmo :Wokonza njinga za Kapalasa mu limbe🚳
16 EvanzMuzik :Owotcha chips ku mpani pani🥘
17 Phyzix : Onyamura matumba ah Cement pa Hardware 🏋️
18 Afana Ceez: Wogulitsa zakudya ndi zomwela mu Deport ya Lilongwe🍞🥂
19 Malinga :Wotsuka ma Galimoto mu 47🚖🚕
20 Gibo Pearson :Wogulitsa Gondolosi, Mnchape, Nthumbulo🥃
I Onjezerani anu🏃 EveryoEveryone