12/09/2024
Guys kumasamala pofuna kuyankhula chifukwa boma ili ndilosiyana ndimaboma apitawa iyi ndi mcp iyi ndiye osangoti...owoo akuzulani ziwalo zuwa likuswa ntengo kkkkk a governor mukupeza bwanji pano kkkk imeneyo ndi mcp simagawa masweet bolanibe inuyo muli ndi mwayi chifukwa akusiyanibe ndi moyo sanakupheni