Waspars business centre -WBC

Waspars business centre -WBC We buy & sell second hand items

24/11/2023

MWAYI WA MAYENDEDWE FROM LIMBE TO ZOMBA

Omwe mwaitanidwa kuzakachita ma interviews ku zomba pa 27 ndi 28 November, 2023, koma mumapezekela ku Blantyre.... Pali mwayi wa mayendedwe ndi K10,000 yokha basi... Muzapita nkuzabwelelanso...

Chiwerengero cha anthu Ofunika ndi Asanu ndi awiri okha (7)

Pozakwelera ndi mu Limbe at PETRODA FILLING STATION.


Those interested tipezeni ku inbox mwachangu ndikusimikiza za ulendowu.

Please ndikuti ku Zomba pa 27 ndi 28 November!

0990558633
0884408915(WhatsApp)

VW machine awa for saleCall/ wap 0884408915Location: BlantyrePrice: 9.5 million
23/03/2022

VW machine awa for sale
Call/ wap 0884408915
Location: Blantyre
Price: 9.5 million

Nissan TeanaGoing@ 1.5 millionAutomatic transmissionBlantyre Bangwe
26/12/2021

Nissan Teana
Going@ 1.5 million
Automatic transmission
Blantyre Bangwe

Toyota CarinaMuli 5A engineAutomatic transmissionWith invalid papersGoing@ K900,000Bangwe nthandizi
30/01/2021

Toyota Carina
Muli 5A engine
Automatic transmission
With invalid papers
Going@ K900,000

Bangwe nthandizi

Sale!! Sale!! Sale!!Toyota bulb shapePrice_ Negotiable!!
23/08/2020

Sale!! Sale!! Sale!!
Toyota bulb shape
Price_ Negotiable!!

Sale!! Sale!! Sale!! 3.5 million
23/08/2020

Sale!! Sale!! Sale!!
3.5 million

Wakutsina khutu ndi mnasi
24/04/2020

Wakutsina khutu ndi mnasi

Munyengo Ino ya corona Ife a WASPARS CAR HIRE titakhala pansi tagwilizana zotsitsa mitengo yobwelekela galimoto zathu ng...
24/04/2020

Munyengo Ino ya corona Ife a WASPARS CAR HIRE titakhala pansi tagwilizana zotsitsa mitengo yobwelekela galimoto zathu ngati njira imodzi yochepetsera kuthithikana kwa ma passengers minibus komwe kuli kuyika miyoyo ya amalawi ambiri pa chiwopsezo chotenga nthendayi

24/04/2020

Tili ndi ma screen ma inches a 14, 20, 21 omwe tikugulitsa pamtengo omvelera choncho Ana asalephele kuwonela mademo, mpira mifilimu ndi nkhani za corona nyumba mwathu chifukwa cha liwuma osafuna kukhala ndi zithu zanu zanu m'manyumbamu

Ife a WASPARS BUSINESS CENTRE tili ndi ma led Tv amtundu wa GEEPAS omwe tikugulutsa pa mtengo wa K150,000 okha, ma TV am...
24/04/2020

Ife a WASPARS BUSINESS CENTRE tili ndi ma led Tv amtundu wa GEEPAS omwe tikugulutsa pa mtengo wa K150,000 okha, ma TV amenewa ndi mtengo wapatali oti kugula lero m***a kugwilitsa ntchito kwa zaka 10 popanda vuto lililonse

24/04/2020

We do as follows:

1. COMPUTER SERVICES
- typing & printing
- graphics desgning
- scanning & photocopying
-we also buy & sale computers & its accesories,
- expert in software & hardware

2. AUDIO & VIDEO PRODUCTIONS
- Poetry, jingles & commedies etc,

3. WASPARS CAR HIRE
with affordable prices

4. We also repair home gadgets

TIMAGULA NDI KUGULITSA MA TV, COMPUTERS BOTH LAPTOPS & DESKTOPS AKUFA OLO ZA MOYO

Address

Wasparscompanion@gmail. Com
Blantyre

Telephone

+265884408915

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Waspars business centre -WBC posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share