Andy P Mw

Call Directions Website Contact the business

Andy P Mw ANDY P is a malawian hip-hop artist

17/10/2026

Dear Lord thank you waking me....wadzuka bwanji nzanga mbali imeneyo?

゚viralシfypシ゚viralシalシ

🖊▶️📝 Nyimbo zinaimbidwa kale zilipo kodi angati mungakonde kuti tiyambe kutulutsaso nyimbozi? ndikuoneni ku comment sect...
16/10/2026

🖊▶️📝 Nyimbo zinaimbidwa kale zilipo kodi angati mungakonde kuti tiyambe kutulutsaso nyimbozi? ndikuoneni ku comment section.


16/10/2026

Last Sunday pa mpila stadium 🏟 nyasa big bullets vs eagles

15/10/2026

Original Gucci sandal going @ 25k blantyre Limbe call/WhatsApp +265887033004

゚viralシfypシ゚viralシalシ

Ambuye amasamala ukavutika usaone ngati wakutaya dziwa kuti ali nawe cholinga....ku ntchito tabwelako tsiku lanu latha b...
14/10/2026

Ambuye amasamala ukavutika usaone ngati wakutaya dziwa kuti ali nawe cholinga....ku ntchito tabwelako tsiku lanu latha bwanji abale?

Stella M Chisale  Tony Collins Banda  Christopher Langwani  Yamikan Linje  Innocent Banda Majawa congratulation guys ma ...
14/10/2026

Stella M Chisale Tony Collins Banda Christopher Langwani Yamikan Linje Innocent Banda Majawa congratulation guys ma likes and comments anu ndimawaona ponyani ma numbers wo tigawane airtime THANK YOU

Pakayenda bwino m'mawa pa mudzi pano anthu 5 amwayi mupata airtime....mukhale ndi usiku wabwino ZIKOMO
04/10/2026

Pakayenda bwino m'mawa pa mudzi pano anthu 5 amwayi mupata airtime....mukhale ndi usiku wabwino ZIKOMO

This was November 26 2021 after anemwe kulandila call from  Banda Jr waku Times 360 Malawi kenako nadzangonva anthu akun...
04/10/2026

This was November 26 2021 after anemwe kulandila call from Banda Jr waku Times 360 Malawi kenako nadzangonva anthu akundiuza kuti ndili mu news paper day iyi 🤣 nali okondwa kuona komwe ndachokela kupusha music mpaka kukapedzeka mu news sizinali zophweka aka kanali koyamba kupedzeka mu news muzonse timayamika YAWEH👏.

04/10/2026

🙄 nde ukhale kuti zomwe ukuphika nzomwe zinatsala eeeh💔🤣

04/10/2026

Good morning FAMILY and friends out there have a blessed Sunday

Address

Blantyre High Way
Blantyre
ANDYPOFFICIAL

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Andy P Mw posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Andy P Mw:

Shortcuts

Share