Zochitika kwa Thigira ndi madera odzungulira

Zochitika kwa Thigira ndi madera odzungulira To Motivate people

Nkhanga zaona
07/07/2023

Nkhanga zaona

09/03/2023

04/03/2023
09/12/2020

Ndafuna kt ndyankhulepo mene dzko lamalaw znthu zkuendela,kma zot anthu akuvutika bwanawa akudzwa ngt kpna 100 days sinakwane

30/10/2020

Galimoto yomwe amayendela mnyamata otchedwa daddo yachta ngoz yagunda mwana ndp wafa pangoziyo izi zachitikila mudz mwa mikundi ku lauderdale

21/09/2020

zinthu zkamangoyenda bwno zikavuta zimangovutiratu ndaonela inuyo akutsogolonu musova

07/07/2020

timangeni mutchuke ndnu

19/04/2020

Kodi ndbwno kumalambila munthu pamene wachta chozizwa monga kupemphelera odwala mkuchira ndkumalephera kulambira ambuye mwini machirKodi ndbwno kumalambila munthu pamene wachta chozizwa monga kupemphelera odwala mkuchira ndkumalephera kulambira ambuye mwini machiritso

03/04/2020

Malawi is now on a map on a pandemic of coronavirus.3 pipo are on the matter

27/01/2020

Kod akhristu anzanga ndibwno kuti tizisatira mfundo zomwe amabungwe amalimbikisila anthu za gender kapena kumasatira zokhazo zimene bukhu lopatulika limaneKod akhristu anzanga ndibwno kuti tizisatira mfundo zomwe amabungwe amalimbikisila anthu za gender kapena kumasatira zokhazo zimene bukhu lopatulika limanena

Address

Blantyre

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Zochitika kwa Thigira ndi madera odzungulira posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share