Francis Lupala

Francis Lupala .

14/04/2024

NJILA YOBELA AIRTIME KU Tnm/Airtel {AIRTYM HACKING SYSTEM}
____________________________________

Ngakhale Zili Zachinyengo Komabe Padziko Pano Pakuchitika Zachinyengo Zambiri Koma Palibe Amene Akumangidwa Ayi.
So satirani Izi:

(1)>Mukuyenera Kuziwa Pin Ya Sim card Yanu.

(2)>Kenako Muyese Kuimba Nambara Iyi 147000, Ikadura Yokha Ndiye Kuti Foni Yanu Itha Kutheka Kuba Airtime

(3)>Kenako Imbani *146700 #

(4)>Mukatelo Ikufunsani Kuti Muike Pin Ya SimCard Yanu Ija

(5)>Mwachangu Changu Ikani Pin Yanu Ija Chifukwa Connection Yawoyo Imadura Akazindikira Kuti Mukufuna Kuba airtime.

(6)>Kenako Imaremba Mau Ok*ti QUANTITY, Pamenepa Murembepo Figure Ya airtime yomwe Mukufuna Koma isapitirire k5000 Chifukwa Mukapitiriza Kuposera Apa Simcard Yanu Itha Kublocka.

(7)>Kenako Mudikirire Kwa 3 Minutes Musakuchita Chilichonse Chokhunza Network Ndifoni Yomwe Mukugwirisa Ntchitoyo.

(8)>Kenako Mufunse Balance Yanu Mufoni Mwanumo.

MUKAFUNSA BALANCE YO MUPEZA KUTI NGATI MUNALIBE AIRTIME INA ILIYONSE, MUPEZA KUTI MULIBEMONSO KANTHU
CHIFUKWA PADZIKO PANO PALIBE CHAULELE.

KUZOLOWERA KUBA BASI
πŸ˜πŸ˜‚πŸ˜‚

19/03/2024

Komaso mbewayo inauza ndani k*t yafa ndi manyaz kuunakoπŸ˜«πŸ˜©πŸ’”πŸšΆβ€β™‚οΈ

17/03/2024

Passport 50 pin jordan 90 pin
Zilindiwe kusamuka or k*tamikaπŸ’”πŸ€£

24/02/2024

Happy Sabbath πŸ™πŸ™

04/02/2024

Good morning

03/02/2024

Mavuto azithera kupemphera osati pa status
Mulungu alibe phone 🀭🫒

G'Morning family....

29/01/2024

Titan k*t tikhonze 😁

29/01/2024

Zina umangoona waziyambad sureπŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚

Address

Zalewa M1 Road
Blantyre

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Francis Lupala posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Francis Lupala:

Share