13/07/2023
Hi admin
Pangani post khani mwina a malawi ena anakumana nazo ndipo anapezakothandizika.
Munthune ndine nyamata wa 26 yrs ndili ndi vuto loti ndikagona ndi kadzi ndi makodzera sanga simantha 1 mins ndimakhala nda taya kale.ndeno mwezi yapitayi ndagwira kadzi wa bho wa ku zomba.chibwezichi chikutha mwedzi umodzi nde week yathayi anabwera pa den kudzandiona ndemuziwa munthu ndichibwedzi chake sitinalephere kupanga chisembwere ndeno atanyamuka kupita kwawo madzulo anatumidzira massage kuti sanasangalasidwe ndimomwe nanyengera ati sindumafikapo ndesikuziwa kuti ndimange bwanji chifukwa namuuzapo za vuto limeneri.ndipo sikoyamba kadzi kundiuza mawu amenewa.