Kelmar legend administrators

Kelmar legend administrators Loving Jehovah is de 1st thing in life

14/06/2024

😭😭

Send a message to learn more

04/04/2024

Update: Kalindo akuyankhanso mulandu wina.

Bon Kalindo tsopano akuonekera m'bwalo la milandu komwe akuyankha mulando wopezeka ndi mfuti mopanda chilolezo.

Izi zachitika patangotha mphindi zochepa, Kalindo atangotuluka mu bwalo la milandu komwe amafuna apemphe belo pa mulandu wofalitsa uthenga wa bodza.
-Robert Mbetewa-

04/04/2024



Munthu woyamba m'mbiri ya dziko la pansi yemwe adamuikira impso (kidney) yochokera ku nkhumba pa 16 March, watulutsidwa m'chipatala m'dziko la USA atayamba kupeza bwino.

Malipoti a BBC ati bambo wa zaka 62 Richard Slayman, amutulutsa m'chipatala cha Massachusetts General Lachitatu, chomwe ndi cha sukulu ya ukachenjede ya Harvard mumzinda wa Boston.

Impsoyo ngakhale ili yochokera ku nkhumba, idasinthidwa zina ndi zina mu ukadaulo wa a za sayansi kuti ikhale m'thupi la munthu. Mmbuyomu zoterezi zakhala zikukanika.

Impsoyo imagwira ntchito yofunikira kwambiri pa moyo wa munthu makamaka pochapa magazi ndi kuchotsa zoipa zomwe zimatuluka mu mkodzo.

Anthu ena, ngakhale kuno ku Malawi, akhala akumwalira ndi vuto la impso ndipo omwe ali ndi kuthekera amakachapitsa magazi kuchipatala pafupipafupi, pomwe ena amapita maiko a kunja kukasinthitsa impso.

(Wolemba Mathews Kasanda)
(Chithuzi cha BBC)

04/04/2024

Back to u

13/09/2023

Zikomo photo lab 🚶

13/09/2023

Germany National Team ikufuna ntchito za mphunzitsi wamkulu wa Liverpool yemwe kwawo ndi ku Germany,izi zadza pomwe dziko la Germany litathamangitsa mphunzitsi wawo

Koma Jurgen Klopp wakana kutenga Germany kamba koti ali ndi ntchito yoti amalize ku Liverpool

Mpheketsela zina zikunveka kuti England National Team ikufuna ntchito za Pep Guardiola...

13/09/2023

Breaking news Jordan Sancho wants to leave Manchester united

13/09/2023

Ndingomva za photo lab ND chn guys?

31/05/2023

Wikise1992x Don will drop male song very soon on 2 June this coming Friday

Address

Phalombe
Blantyre
HIP

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Kelmar legend administrators posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Kelmar legend administrators:

Share