27/12/2024
Eeeeeh, kulimakomenti kuseliku. Teddy this Teddy that. Ifeyo nde stingalore muzimuna Teddy wathuyo kuti ngoyendayendayi, ati iyayi, akanazipanga control, Inu zoti control imabooka simunamvepo????๐๐ฅฑ๐๐ฅฑ.
Kodi mawona ngati hmm, nzophweka chifukwa sinu amuna eeti????, man is moved by sight, kungowona nsana timatha kubalalika, Inu amenewo mwagundika ngati munakhalapo wamuna mxieeeee๐๐ฅฑ๐ฅฑ. Chi Nana chija munachiwona bwinobwino koma???? Kapena bax yanu ija yongotokota ija.
Wait kaye, nsanayiwale, tamutengeni girlfriend yo ndi Nana muwayike apa mwina tiyambilenso kuyiwunguza nkhaniyi fukwatu nde eeeeeeh, Teddy mwatinyozela kuseliku๐๐๐ฅฑ๐๐ฅฑ