28/03/2025
🔥 Tetezani Zokolola zanu ndi Grain Guard! 🔥
🚜 Alimi, musalole kuti zirombo ziwononge khama lanu! Sungani mbewu zanu zosungidwa kukhala zotetezeka, zatsopano, komanso zopanda tizilombo ndi Grain Guard—chitchinjirizo chachikulu ku nankafumbwe ndi tizirombo toononga zokolora.
✅ Amapha komanso kuteteza nankafumbwe kuti asawononge zokolola zanu
✅ Mankhwalawa ndi a ufa komanso osavuta kugwiritsa ntchito—ingosakanizani ndi zokolora zanu
✅ Chitetezo chokhalitsa kuti muwonjezere phindu lanu
✅ Ndiotetezeka ku mbewu ndi nkhokwe zosungira
💪 Osayika pachiwopsezo chotaya zokolola zanu-Zitetezeni ndi Grain Guard!