ZWIDE

ZWIDE Real life talk | Money & daily struggles 🇲🇼
Best investment Relatable content every day Follow for more
(1)

Week 1 ya June ija yatha motere Sunbird wasungabe chinthuchi
05/06/2026

Week 1 ya June ija yatha motere

Sunbird wasungabe chinthuchi

Long term ija Omwe agula ma share and akhala nawo kwa Chaka ngakhale ena akulira iwo angoti owowoChifukwa even ma share ...
05/06/2026

Long term ija

Omwe agula ma share and akhala nawo kwa Chaka ngakhale ena akulira iwo angoti owowo
Chifukwa even ma share price wo atsika koma pomwe anagulirira iwo ali kutali
Mwezi ngati omweuno

Share ya FMBCH inali pa K904

Yatsika pano ili pa K1 648
Ndekuti akadalibe ndi phindu loposa 74%

Standard bank inali pa 1 sau nkanthu pano yatsika ikadali pa 3 sau nkanthu still 70% gain

NBS inali pa K335 lero ili pa 742 over 120% gain

Yanu yapanga loss zingati since June last year?

Kapena since June last year? mwapanga gain zingati?

Image: Daily summary ya pa 5 June 2025

05/06/2026

Pa Mainboard Unofficially
CDH
MAIIC
Centenary

Always With You
04/06/2026

Always With You

Ma tally
04/06/2026

Ma tally



FDH Financial Holdings has disclosed that its newly acquired Mozambique business is yet to start contributing to the group's earnings.

Managing Director, Noel Nkulichi, has disclosed during the company's 19th Annual General Meeting in Blantyre, where he said the Mozambican subsidiary has remained loss-making due to regulatory restrictions that had been imposed on the institution before its acquisition.

He, however, said the company has already embarked on a turnaround strategy aimed at restoring the bank to profitability so that it can begin contributing positively to the group's financial performance.

FDH Acquired 98.87% stake in Ecobank Mozambique, which now operates as FDH Mozambique SA.

By Earlene Chimoyo

04/06/2026

Ma shareholders a OMU suti timakusalani ai inu ndi ma bigger
OMU bho?

Company imapanga declare dividends ngati company yo yapanga phindu and ili ndi cash pa phindu lapangaloHealth ya company...
04/06/2026

Company imapanga declare dividends ngati company yo yapanga phindu and ili ndi cash pa phindu lapangalo

Health ya company imaoneka pomwe ikupitiliza kupereka ma dividends regularly

Health ya company sioneka pomwe share price ikutsika kapena kukwera kwambiri

Izitu nchifukwa chake Ma company akupitilizabe kugawa ma dividends ngakhale ma price a share yawo akutsika

Inu mubazifunsapo kuti
Why?

Ngati company ikugwa ingamagaweso phindu?

04/06/2026

FDHB plc Shareholders
Lero waku Mpemba tikakumane kumeko tikudziwana

Dividend nkuzakwera ndi 128.6%Ndalama zikupangidwa Sugar sugar
03/06/2026

Dividend nkuzakwera ndi 128.6%

Ndalama zikupangidwa
Sugar sugar

Tawerukako NITL pa front apoNBM nayo mbuyomo
03/06/2026

Tawerukako NITL pa front apo

NBM nayo mbuyomo

Address

Blantyre

Telephone

+265998838518

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when ZWIDE posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to ZWIDE:

Share