12/12/2021
Team ya Jihad yochokera mmudzi mwa Ntapa, group village chikapa T/A chikowi, Zomba ikuitana azitsogoleli a ma team monga : Asernal, Aire mafumu, Kambuku, Young soccer, Sande, Trouble komanso Lambulira kuti adzakambirane za ndondomeko ya bonanza yomwe idzachitike motere:
Tsiku :lachiwiri
Malo: new langers ground
Nthawi :2:00 madzulo
Ochititsa: ma sponsors a team ya Jihad.
Chonde zatsungeni nthawi komanso musazaiware kutenga entry fee yokwana 3 000 kwacha.
Jihad Fc kulimbikitsa achinyamata kutalikana ndi zoipa!