M.C.P Chipani Changa

M.C.P Chipani Changa This Is An Official Page For The Politics In Malawi

25/09/2025

Moni Amalawi Anzanga

Maka kwa Onse Omwe mumatsatira page lino

poyamba ndikufuna ndipeleke mafuno abwino kwa alpha peter Munthalika posankhidwa kukhala president wa dziko lino la malawi 🇲🇼
Mulungu akutsogolereni pomwe mukhale mukugwira ntchito yomwe Mulungu wakupatsani Kachikena

Amalawi zisankho zantha mpikisano uliwonse pamakhala munthu mmodzi wopambana ndipo panopa Amene mulungu wasankha ndi Amunthalika

Tiyeni tonse ngati Amalawi tigwirane Manja kuti malawi wanthuyu Apite chitsogolo

palibe munthu wina angabwele kudzatukula malawi ngati ife Eni ake sitichilimika

zilibe kanthu kuti amene wasankhidwa kukhala mtsogoleri wadziko si amene inu munamukonda dziwani kuti sizokkhumba zilizonse zomwe ife timafuna ndikukwanilitsa Ena amafa akulakalaka kudzapita dziko Lina koma maloto awo osakwanilitsidwa

Zina mulungu amazilora mwadara kuti zisachitike pa moyo wanu ndicholinga

ife tonse amene timatsatila chipani cha malawi congress tisataye mtima next time zidzayenda ndikudziwa mwaluza zinthu zochuluka ndalama zoti mukanatha kulimitsila kumunda koma zonse zapita chonde Osadzipha kapena kudzitembelera kupena kudzionera pansi nthawi ilipo zidzayenda

MALANGIZO KWA AKULUAKULU ACHIPANI CHA MCP

Dziwani kuti zinthu izi ndizomwe zatipangitsa kuti Tigonje pazisankho zangothazi

1:Kukwela kwa zinthu zofunikira Maka zipangizo za ulimi komanso zinthu Zina zofunika pamoyo wa munthu wa tsiku ndi tsiku

2:KUSAGANIZILA MOYO WA anthu ogwira ntchito m'boma pomwe zinthu zinafika povuta kukwela mitengo ya katundu Ma salale a wanthu ogwira ntchito m'boma anali Ochepa

3:KATANGALE KAPENA KUTI KUBA Kopanda nako Manyazi komangofuna zonse zikhale zanu kuiwala omwe anakuvotelani

4:IMFA YA CHILIMA NDI ANTHU ENA 8
Kaya munatengapo gawo kapena ayi izi ndichinthu chimodzi chomwe anthu sadzakuiwalani mpaka kalekale

5:KUSOWA KWA MAFUTA AGALIMOTO
munthu kuti ayende,adye ndikuchita ma business amadalira Mafuta

6:ZIPHASO ZOTULUKIRA KUNJA KOMANSO ZIPHASO ZOYENDERA PA MSEU

Nthawi ilipo ndipo Osataya mtima omwe akukanani ndi Ochepa omwe akuvotelani ndi ambiri chikhoza kukhala chitonzo pa moyo...
24/09/2025

Nthawi ilipo ndipo Osataya mtima omwe akukanani ndi Ochepa omwe akuvotelani ndi ambiri

chikhoza kukhala chitonzo pa moyo wanu koma tsiku Linaso mudzasimba lokoma

24/09/2025

Shout out to my newest followers! Excited to have you onboard! Emmanuel Mbingwani, Wedson Chipiliro, Bless Magana, George Vigro, Aizeck Kamanga, Mayamiko Sakali, Anold Mw, Millicah S. Peter, Hp Auleliano, Faddah Chibowa, Humphreys Unique, Jimmy Hau, Maku Gayes, Doctors Simba, eky idaz, Judifi Manyenje, Giboh

Congratulations APM💥💥💥
23/09/2025

Congratulations APM💥💥💥

22/09/2025

Big shout out to my newest top fans! Kulinji Tambala, Bickton Maidon, Mar Sambo, Josophart Kalumikiza, Collings Banda

22/09/2025

Ngati silero koma Mawa zidzayenda

20/09/2025

Mkazi akapanga chiganizo choti wakutaya ndipo za iwe sakuganizilanso

I think it's better kuvomeleza msanga ngati sutelo

Umatha zako zonse mkumunyengelera chonsecho za iwe anaiwala kalekale

15/09/2025

Amene akufuna ma T-shirt oti tikavale pa tsiku lolumbilitsa chakwera mundiuze

Ena ndawagaila kale chonde pokumana mukudziwapo mulilongwe

13/09/2025

Ndikufuna anthu okwana 500 Omwe tidzachoke kuno ku mwera transport ilipo tidzapite kolumbilitsa chakwela chonde

Lembani dzina lanu chakudya chilipo komanso pobwela mudzalandila kenakake

Magalimoto alipo aulele

Kuti izi zitheke dzavoteleni chakwela kenako

Tizidzanyamuka

Please Lembetsani mainawo

Address

Lunzu
Chileka
1990

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when M.C.P Chipani Changa posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to M.C.P Chipani Changa:

Share