Tsugah Tsuu

Tsugah Tsuu FreeForTime
(1)

Mwina mumangonva kuti ku Kasungu kuli kuDam komwe zibwezi zimakumanilana nde ndikumenekutu abale kuDam.
02/09/2026

Mwina mumangonva kuti ku Kasungu kuli kuDam komwe zibwezi zimakumanilana nde ndikumenekutu abale kuDam.

02/09/2026

Nkhani za akazi sitisekana.

Koma mukadatipatsako mpata kuti tisiyeko mowa, nanga uwu nde mwawubweletsaso liti.
02/09/2026

Koma mukadatipatsako mpata kuti tisiyeko mowa, nanga uwu nde mwawubweletsaso liti.

02/09/2026

Chibwezi changa chitangondigulirako ka jersey kamodzi koma ndingasangalare bwanji 🙌

Umazaziona ngatitu uli nditimaluso tingapo pomwe uli osathandiza.
01/09/2026

Umazaziona ngatitu uli nditimaluso tingapo pomwe uli osathandiza.

Chidabwera kuukwati koma ngati nkwatibwiyo sadali ex wake nde ndi mwayi.
30/08/2026

Chidabwera kuukwati koma ngati nkwatibwiyo sadali ex wake nde ndi mwayi.

Zochitika zawumadafaka
29/08/2026

Zochitika zawumadafaka

29/08/2026

Ngati ku Bet mukungoluza vomekezani simungalemele ndi njunga tiyeni tikakwime.

Good morning

Ana ajajah.
28/08/2026

Ana ajajah.

Ma disco nde mwativinitsa ochuluka m'mudzimu ulemu wanu madhala. Happy birthday Junior.
28/08/2026

Ma disco nde mwativinitsa ochuluka m'mudzimu ulemu wanu madhala. Happy birthday Junior.

Address

Kasungu

Telephone

+265999559233

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Tsugah Tsuu posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share