Nathenje Entertainment

Nathenje Entertainment The Official page for Nathenje Entertainment and Nathenje Music Awards

31 of may
25/05/2026

31 of may

🌈 Tili bhobho kamofi.
11/05/2026

🌈 Tili bhobho kamofi.

Nathenje info. Boma lati likugulitsa ndege ili mu chithunziyi yomwe eni ake anangoyisiya pa bwalo la Kamuzu kwa zaka 17 ...
28/04/2026

Nathenje info.

Boma lati likugulitsa ndege ili mu chithunziyi yomwe eni ake anangoyisiya pa bwalo la Kamuzu kwa zaka 17 tsopano.

Nduna yoona za Mtengatenga a Jappie Mhango, yauza Zodiak Online, boma lakhala likusaka eni ndegeyi koma sakupezeka ndi chifukwa akuyigulitsa chifukwa ikusokoneza ntchito za pa bwalo la KIA.

A Mhango ati nzodandaulitsa kuti anthu ena akuona ngati ku Malawi kuno nde kotayira zinthu zawo chifukwa oyendetsa ndege atatsitsa katundu anakwera ndege ina n'kumapita osabwereranso.

(Report by dj born nathenje Entertainment)

Zonena zambiri tilibe.. Ambuye odziwa kutothoza atothoze banja la a Mwasiya.. May her soul rest in peace 💔
28/04/2026

Zonena zambiri tilibe.. Ambuye odziwa kutothoza atothoze banja la a Mwasiya.. May her soul rest in peace 💔

Let's party.
28/03/2026

Let's party.

18/03/2026

Agulu.

Mawa zipona uku
06/12/2025

Mawa zipona uku

  entertainment.@ #Woyimba Patience Namadingo ndi yemwe alandire mphoto zambiri ku mwambo wa chaka chino wa UMP Music Aw...
26/11/2025

entertainment.@ #

Woyimba Patience Namadingo ndi yemwe alandire mphoto zambiri ku mwambo wa chaka chino wa UMP Music Awards.

Namadingo alandira mphoto monga Artist of the year(Male), Song of the year Tuli, Best Humanitarian komanso Best Live Act.

Eli Njuchi komanso Tay Grin ndi omwe atsatira ndipo Eli alandira mphoto monga Album of the year Cifu komanso Best Afro-beats/Fusion Act.

Pomwe Tay Grin alandira mphoto monga Tourism Promotion Award komanso Global Impact Award.

Enanso omwe apambana ndi monga Jetu ngati Artist of the year (Female), Wyson Malakamu mnyamata wa Aumvere fungo ngati Best Innovative Sound, Joe Ikon ngati Best Amapiano Act, Masintha Women Choir ngati Best Gospel Act, Black Missionaries ngati Best Band.

Mwambo wopereka mphotozi uchitika mu mzinda wa Blantyre pa 20 mwezi wamawa.

(Wolemba born Chakhwantha)

Address

Nathenje
Lilongwe

Telephone

+265990424332

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Nathenje Entertainment posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Nathenje Entertainment:

Share