Falcon Gas Malawi

Directions Contact the business

Falcon Gas Malawi Our Mission is to supply Affordable, Safe and Reliable LPG for Domestic and Commercial Use in Malawi

Lero tili pa Wakawaka Market,tabwerani kuti mupeze gas cylinder.Tiri ndi ma 5kgs,9kgs & 12kgs. Zonsesi pamtengo osaboola...
28/08/2026

Lero tili pa Wakawaka Market,tabwerani kuti mupeze gas cylinder.

Tiri ndi ma 5kgs,9kgs & 12kgs. Zonsesi pamtengo osaboola mtengo.

Zabwino tirinazo, ku Falcon Gas tikupezekaso ndima 9kgs cylinder amene amabwera ndi gas kale.Inu kodi zabwino simmazifun...
25/08/2026

Zabwino tirinazo, ku Falcon Gas tikupezekaso ndima 9kgs cylinder amene amabwera ndi gas kale.

Inu kodi zabwino simmazifuna, tiyimbireni phone lero kuti inunso mupeze yanu mwachangu.

0889939000

Amzanu dzulo anapeza nawo mwayi ogula 5kgs Cylinder, m***a kuwona mmene anakondwera 🔥🔥🔥🔥🔥Inuso mwayi mulinawo kuti m***a...
15/08/2026

Amzanu dzulo anapeza nawo mwayi ogula 5kgs Cylinder, m***a kuwona mmene anakondwera 🔥🔥🔥🔥🔥

Inuso mwayi mulinawo kuti m***a kupeza yanu lero pamtengo wa k130,000 yokha basi.

Tiyimbireni phone pa 0889939000

Congratulations to Scorchers pofika ndime yotsiriza ya Wafcon.Kwa inu akasi,osathamangira malo amene sakhala ndi gas kom...
13/08/2026

Congratulations to Scorchers pofika ndime yotsiriza ya Wafcon.

Kwa inu akasi,osathamangira malo amene sakhala ndi gas koma kukuuzani nthano nthawi zonse ngati Team ya Algeria🌝🙌😂

Sankhani Falcon Gas lero ndipo mudzakhala moyo osangalala nthawi zonse ngati Sikochazi yathu inu aaaaaa🔥🔥🔥

Tayimbani phone mwachangu kuti mudziwe zambiri #0889939000 #

Mpira kuti ukome madzulo ano,zikufunika muphike nthawi yabwino komanso mwachangu. Tipezeni ku Falcon Gas kuti mudzathiri...
12/08/2026

Mpira kuti ukome madzulo ano,zikufunika muphike nthawi yabwino komanso mwachangu.

Tipezeni ku Falcon Gas kuti mudzathiritse gas, komanso kupeza mwayi wa ma Cylinders athu apamwamba.

Tikupezeka ndima 5Kgs,9kgs ndi 12kgs onsewatu pamtengo osaboola mthumba.

Tiyimbireni phone kuti mupeze yanu mwachangu🔥🔥🔥🔥🔥

0889939000

Happy customers🔥🔥🔥All the way from Dedza, apeze awo ma 5kgs cylinders, inu tikubweretsereni kuti akasitomala 🌝Tiyimbiren...
10/08/2026

Happy customers🔥🔥🔥

All the way from Dedza, apeze awo ma 5kgs cylinders, inu tikubweretsereni kuti akasitomala 🌝

Tiyimbireni phone pa 0889939000

Yambani tsiku lanu pogwiritsa ntchito katundu wabwino ochokera ku Falcon Gas.Musayiwale tikupezeka ndima 5kgs Cylinder a...
05/08/2026

Yambani tsiku lanu pogwiritsa ntchito katundu wabwino ochokera ku Falcon Gas.

Musayiwale tikupezeka ndima 5kgs Cylinder amene akugulitsidwa pamtengo osaboola mthumba.

Imbani phone kuti inuso mupeze yanu mwachangu.

0889939000

Okondedwa ma Kasitomala athu, tafuna tikudziwitseni zakusintha mtengo kwa 5kgs Cylinder yathu imene last week inayikidwa...
03/08/2026

Okondedwa ma Kasitomala athu, tafuna tikudziwitseni zakusintha mtengo kwa 5kgs Cylinder yathu imene last week inayikidwa pamtengo wa k127,000.

Koma panopa yafika pa k130,000, kusinthaku kwadza kamba kakukwera mtengo wa Gas umene walengezedwa ndi Boma Loweruka lapitali.

Mukufuna kudziwa zambiri tiyimbireni phone pa 0889939000 kuti inuso mupeze mwayi wa Cylinder.

Weekend nde yayandikira, simungazepule mwadongosola ngati mukuphikirabe makala.Takubweretserani ka 5kgs Cylinder kamene ...
30/07/2026

Weekend nde yayandikira, simungazepule mwadongosola ngati mukuphikirabe makala.

Takubweretserani ka 5kgs Cylinder kamene kakupita pamtengo osaboola nthumba ndi k127,000 yokha inuyo mukhala mwaphweketsa moyo wanu.

Imbani phone pa 0889939000 kuti mupeze yanh mwachangu.

Get your gas cylinders at affordable price.  Please take note; 6kgs and 48kgs are out of stock.Remember we do free home ...
09/01/2026

Get your gas cylinders at affordable price. Please take note; 6kgs and 48kgs are out of stock.

Remember we do free home deliveries only to those using Falcon cylinders and are within Lilongwe

Come grab yours today!😊we are located in Kanengo opposite Coca-cola Company.

Address

Plot 29/Area 39, Kanengo, Along Salima Road
Lilongwe

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Falcon Gas Malawi posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Falcon Gas Malawi:

Shortcuts

Share