Soulmates Malawi ZONE

Soulmates Malawi ZONE Connecting singles to their soulmate for serious relationship or for friends with a benefits and any other form of love connection

04/10/2025

After kusowa ndi campaign now am back to business

Lilongwe Chisapo Pali mamuna wina akuna mkazi wa hit n run lero nde ngati alipo mkazi akufuna ndalama andipeza ku inbox

20/05/2025

Hello Admin,,

Ndiye mamuna ndafika ku town ya Balaka lero nde ndikufuna mundipezele mkazi oti akukhala mozungulila Balaka or Zomba kuti zimvana naye , zaka zilibe ntchito bola akhale odziwa chomwe akufuna , ine ndili zaka 35

Serious ladies inbox admin for connection

11/05/2025

MZUZU

Am the same woman ndinakutumizilapo message yoti ndikufuna mamuna koma sizinayende, ndine mzimayi wazaka 43 ana 2, Hiv positive namuna akhale wazaka 48 above ndi uli ku Mzuzu

Ngati uli mamuna ofuna mkazi wa serious komaso oti Ali zochita nde ndi emeneyu , tipezeni ku inbox

18/04/2025

Hello Admin

Tayesa kusaka mkazi wa serious koma sakupezeka nde apa ndakhalitsa kufuna kusitha oil nde mwa Chocho ndipezeleni mkazi oti abwele kwathu kuno lero azagone ndimuona Ina yake ine ndili mowandikana ndi Nguludi turn off nde akhoza kukhala wa around or near by areas monga Bangwe , Goliati , Mkando ndi Madera ozungulila akapezeka mundiuza

30/01/2025

Chaka chanu munachilowa bwanji ndipo chikuyenda bwanji?

25/12/2024

Mamuna zaka 40 ku Thyolo, Goliati akufuna mkazi wa serious zaka 20 to 50 , mamunayo amagwira ntchito, serious ladies inbox admin

27/11/2024

Nyamata wa zaka 30 akufuna mkazi wa chibwezi ku Lilongwe, sakusakha zaka bola mkazi basi, mamunayo amagwira ntchito

18/11/2024

Admin tinthandizeni kuno kusalima ndinayamba Karen kudandaula apa wakufuna kwabwino andiponyereko ka ndalama nyumba yang yasasuka ndilibe kolowera katundu wanyowa ndimafunako 12 pin pang Ono pangono nambala ndi iyi 0986901915 chonde chonde ndikunana ndipereke rent akundinthamangisa Adam ndiyang Ana inu

31/10/2024

35 yrs man based in Lilongwe is looking for serious lady for serious relationship, aged is just a number

09/10/2024

Mamuna waku Blantyre zaka 40 akufuna mkazi wa serious around Blantyre, serious ladies inbox admin

01/10/2024

Primary xul teacher based in Chiradzulu aged 47 is here looking for serious lady to marry and the lady should be based in either of the following areas; Blantyre, Thyolo, Zomba or Mulanje working or business if interested in this man inbox admin for connection

23/09/2024

BLANTYRE

Mamuna wa zaka 35 akufuna mkazi wa serious oti kuyamba naye chibwezi chokathela banja , mkazi akhale wa ulemu ndi omvela mwambo mkazi wa malire zaka 50 age is just a number nkhani chikondi ndi kumvetsetsana

If interested in this man inbox admin for connection

Address

Lilongwe

Telephone

+265888856673

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Soulmates Malawi ZONE posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share

Category