Pemphero Mphande

Pemphero Mphande Author and a community worker by heart

Morning praise team,Lero ndi tsiku lomaliza mwezi uno kupereka ngongore amene anatsala osatenga dzulo ndipezen inbox ler...
23/01/2026

Morning praise team,Lero ndi tsiku lomaliza mwezi uno kupereka ngongore amene anatsala osatenga dzulo ndipezen inbox lero kuti nanu muthandizike ndi ngongole za online zimenezi.

Appline 0998005691

Hello Mr p  please post for me I'm looking for a serious lady to marry,I have two grown kids and they independent,I'm HI...
22/01/2026

Hello Mr p please post for me I'm looking for a serious lady to marry,I have two grown kids and they independent,I'm HIV positive so I need a positive woman tool,I work under reserve Bank of Malawi,please post my picture ndikufuna wondikondayo andiwonere2.

Yemwe alindi connection fee yo andipeze inbox ndimupange connect WhatsApp number 0998005691

21/01/2026

Please hide me,Neba wanga amamenyana ndi mkazi wake dzulo madzulo. Ine ndinathamangira konko kukawaleretsa chifukwa amayiwo amati atolacho chimakhala chida chomenyela amuna awo. Mwatsoka ndinakhudza stand ya TV and plasma yawo inagwa pansi ndikuphwanyika. Panopa anabwera kundifunsa kuti za TV yawo zilipati,Nditani pamenepa? 🙆🙆

Special connections ndimafuna anthu omwe ali single  ndipo anatopa ndikukhala okha andipeze inbox ndiwapange connect ndi...
19/01/2026

Special connections
ndimafuna anthu omwe ali single ndipo anatopa ndikukhala okha andipeze inbox ndiwapange connect ndima singlesoul anzawo,mudzitumiza ma details anu onse komanso amunthu yemwe mukufuna.

Please sidza ulele ngati ulibe connection fee usandi vutitse ku inbox ku,0998005691

18/01/2026

Sunday, 17th January Blantyre. Story 2
-----------------------------------------------------------------

Yes, boss. Am a 38 years old man, married Based in Lilongwe.

Mundipangirako post hope it fit to mystical Sunday boss. K*k

So in 2008 I got 37 points in MSCE exam even although ndimabwelenza kachitatu. So my mum was told kuti nalozedwa nzeru zanga zinalokedwa ndi anzawo anawauza ndipite kwa sing'anga. So ananditengera kwa sing'anga ku Rumphi amene anaombeza ndikunena kuti mizimu yakwathu inasankha kuti ineyo nditenge mutu ngati agogo anga apatali amene anali ouma mutu naonso. Sing'anga anawatchula dzina agogo angawo but no one knew him its like he was my great great great grandfather only my grandma claim that the name sound family. According to witchdoctor, akuti our ancestors asign mind ya our old ancestors to one of us. Nde my siblings who was intelligent taken after enawo. Now this witchdoctor anandicheka mphini zitatu mu mutu ndikundiuza kuti pa next MSCE exams ndikalembetse dzina la agogo anga akalenso amene anawatchula dzina he said amenewo was very intelligent. But again no one knew him. So 2009 MSCE exams I change my name in msce and use this guy's name who I don't know, napezabe bad results 34 points. Even although the witchdoctor said ndizakhoza below 10 points kkkk. Fastforward, now I have son who always bottom of class and zikundidesa nkhawa chifukwa olo kulemba ndi kuwerenga akuvutika. Mwanayu ali ndi dzaka 11. I told my mum so anapita kwa sing'anga yemwe uja and he say akuti nzimu omwe unalowa mwa ine of failure uja unakwiya nditasintha dzina nde walowa in my son and he making it worse . Now solution i should change my son's name to jnr like after me which is the same name as my ancestor wa nzeru uja. Koma ineyo am now doubting. Kuti izizi ndizoona ?? Kapena anthufe ndiouma mutu basi? What should I do. Chifukwa ineyo paja nali ouma mutu and my wife too anali ouma mutu....

18/01/2026

Sunday, 17 January. Blantyre. Story 1
---------------------------------------------------------------
Mundiponyeleko pa mystical Sunday. Ndine mtsikana kuno ku BT. Ndili ndi dzaka 28. Ndili ndi nzanga amene timapanga limodzi business ya katapila. Timabwelekesa ndalama. Nde pali bambo ena ake ndi aphunzitsi mu Blantyre muno anabwereka 200 like 3 months ago mpaka inakula mpaka 2.4 million. Ndiye last week tinakalanda ma TV ,fridge ndi cooker chifukwa iwowo amati interest yakuluka amafuna angolipira 500 pin kenako tithane. Kom okha anasaina kuti ifike pa 2.4 mita,. Ndiye titalanda katundu tinakamusiya kunyumba kwanga. Mamawa ntazuka nadabwa kuti katundu yo sindikumuona....koma wanga analipo,,kukhomo koseka. Ndinamuimbira nzanga uja anabwera kenako tinaimbira aphunzitsi aja. Titawafunsa anati paja Nokia mwazasiya katundu pakati pa usiku. Ine mantha anandigwira...,,,tinapita kwao tinapeza katundu alibi kwawo. After kukangana tinautengaso,,,nanga si ndimaona ngati anazubaso. koma mamawa onse unachokanso. Apa naziwa kuti zamuwanthu. Anatiuza mwa challenge kuti ine ndikuziwa kuti katundu wanu mwatenga tathana koma titapita kwao katundu anali mu nyumba mwao. Anatipanga challenge kuti utengeni ngati mukufuna katunduwu, tengani ubwelanso. Sono ifeyo tayenda mwa sing'anga kuti atithandize,,,koma onse amangoti mdala amene uja ndiokhwima zomwe anapanga olo ife kupanga mankhwala zitigwera...nde ifeyo tikufuna ndalama yathu at least olo 500 yo chabwino ngati 2.4 mita sitheka. So help us peh with a strong witchdoctor.

Happy birthday to Barack Obama wife.Happy birthday to the woman who lights up every room she walks into. I love you, Mic...
18/01/2026

Happy birthday to Barack Obama wife.

Happy birthday to the woman who lights up every room she walks into. I love you, Miche.

17/01/2026

Hi hide my id and post for me
Since we got married with my wife she don't sq**rt what am I lacking? its been 2 years now but if I go outside have s*x with other girls they do cume, but if I come home and try those same angles with my wife nothing happens until I realise what should I do mr p and you're praise team?

16/01/2026

Mr p chonde undibise ndine mmayi wa pa banja ndinthu, amunanga ali ku joni Mr p page yanu yindithetsela banja muthune nakumana ndi mamuna chifukwa cha kutopa Mr p ndi mwana according ndi size yanga nde namuyitanitsa ku nyumba kwanga kuti azandinyenge ulele coz sitimakhala kotalikana koti bwanji Mr p mnyamata andipanga chipongwe anandijambula nditavula ma pics komanso ma videos komatu Mr p ndri pa mavuto chifukwa mnyamatayi mwezi ndi mwezi akumayitanitsa ndalama ndpo akumapanga demand ndalama yochuruka moti ndatha ndikugalitsa katundu wa nyumba kuopa kuti asandiyalutse amandiuza zoti ngat sindikwanitsa kumupatsa ndalama zomwe akufuna andiyalutsa komanso anatenga number ya amunanga nde amandiuza zoti adzatumiziranso amunanga 😭💔Mr p ndasauka chifukwa cha mnyamata ameneyi moti even amunanga akanditumizira ndalama zikumangopita kwa iyeyo ana anga kumagona ndi njala Mr p ndri pa mavuto ndpo choti ndipange chikundisowa ndimapempheko anthu ako andithandize kuti ineyo ndingapange kuti mnyamata yo asandiyalutse komanso asiye kumafuna ndalama kwaineyo chonde ndithandizeni 😭

16/01/2026

Post for me ,munthune ndine okwatira and mkadziwanga tili ndi Ana awiri ,koma chomwe amachita mkadziyu ndikundipedzera zifukwa ,sitimatha 3 weeks tisanakangane ,ineyo ndatopa ndikhalidwe limenero,ndingatani kt chikondi changa chizichepa mwamkadziyu coz ndimamukonda kwambiri..

Today its 95th Birthday for mr Chalamanda tiyeni tiwathandize kusangalala.
15/01/2026

Today its 95th Birthday for mr Chalamanda tiyeni tiwathandize kusangalala.

Address

Lilongwe

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Pemphero Mphande posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share