Newstart Aquaculture

Newstart Aquaculture We specialized in Agribusiness and Business Management. We aim to support farmers in advanced farming

ZIFUKWA ZIMENE ALIMI AMBIRI A NSOMBA AMALEPHERA PA ULIMIWUZifukwa zomwe alimi ena amalephera ulimiwu Ndi monga; kusowa m...
20/08/2026

ZIFUKWA ZIMENE ALIMI AMBIRI A NSOMBA AMALEPHERA PA ULIMIWU

Zifukwa zomwe alimi ena amalephera ulimiwu Ndi monga; kusowa msika, malo osayenera a famu, kapangidwe ka famu kosayenera, dongosolo losayenera la ndalama (bizinesi), komanso kusowa luso laumisiri.

Zifukwa Zake Mwachidule

1. Kusowa msika: Palibe malo ogulitsira nsomba kapena ogula okwanira pafupi.

2. Malo osayenera a famu: Famu ili pamalo amene madzi Palibe kapena dothi siligwira madzi bwino.

3. Kapangidwe kosayenera ka famu: Mayimbidwe kapena maiwe amangidwa mwaulesi kapena mosasamala madzi.

4. Dongosolo losayenera la ndalama: Kusowa ndalama zokwanira kapena kugwiritsa ntchito molakwika ndalama za bizinesiyo.

5. Kusowa luso laukadauro: Alimi alibe chidziwitso cha mmene angadyetsere, kusamalira, kapena kuteteza nsomba ku matenda.

Ngati mukufuna, nditha kukuthandizani ndondomeko ya mmene mungayambitsire famu ya nsomba yopambana kapena njira zothetsera mavuto amenewa

Imbani kapena tiyakhuleni kudzela pa matsamba anthu a mchezo a WhatsApp kapena Facebook

Phone Calls: +265883075094
WhatsApp: +265883075094
Email: [email protected]
Facebook:
Location: Area 24, Lilongwe.

Your trusted partner in fish farming and water storage solutions.

Follow the NEWSTART AQUACULTURE channel on WhatsApp: https://whatsapp.com/channel/0029VbCE44Z11ulXCqjyVa0x
19/08/2026

Follow the NEWSTART AQUACULTURE channel on WhatsApp: https://whatsapp.com/channel/0029VbCE44Z11ulXCqjyVa0x

Follow NEWSTART AQUACULTURE's WhatsApp Channel. Welcome to Newstart Aquaculture – your trusted source for aquaculture, fish farming, livestock production, pasture management, and agribusiness knowledge.
Our channel is dedicated to empowering farmers, entrepreneurs, students, and agricultural enthusiasts with practical information, modern farming techniques, and innovative solutions that improve productivity and profitability. We share educational content on fish farming, pond management, water quality monitoring, fish nutrition, livestock feeding, pasture development, fodder production, and sustainable agricultural practices.
Whether you are a beginner or an experienced farmer, Newstart Aquaculture provides valuable insights, training tips, and real-life farming experiences to help you succeed in the agricultural sector.
Subscribe to Newstart Aquaculture and join our growing community as we promote sustainable aquaculture, livestock development, food security, and agribusiness excellence.

*_Don't leave anyone behind_*

*_Get ready to insights and knowledge on Morden farming_*

Newstart Aquaculture – Growing Fish, Raising Livestock, Building Prosperity.

Through Morden farming your not limited to farms only. Anywhere else near you can practice farming

Through;

1. Pondliner and Galvanized fish tanks, fish Cages as well as Concrete Tanks
2. Zero Grazing with livestock Production and many more solutions available

Our services and products are offered country wide, Feel free to contact us calls and social media accounts below;

Call: +265883075094
WhatsApp: +265883075094
Email: [email protected]
Facebook:
Location: Area 24, Lilongwe

We Leave No One Behind

Your trusted and reliable partner in fish farming and water storage solutions. Join 189 followers for the latest updates.

We have the solutions
19/08/2026

We have the solutions

PONDLINERPondliner ndi pepala lomwe limathandiza alimi a Nsomba kuwetelamo Nsomba komaso kuthandiza kusungilamo madzi, p...
17/08/2026

PONDLINER

Pondliner ndi pepala lomwe limathandiza alimi a Nsomba kuwetelamo Nsomba komaso kuthandiza kusungilamo madzi, pepalari limaikidwa pa malo pomwe nthaka yake singasunge madzi, munjira monga kukumba pansi pa nthaka komaso kuika pa mwamba pa nthaka

Ubwino wake:

1. Njira imeneyi imalola alimi ang'onoang'ono a nsomba kusunga madzi okwanila pa ulimi wawo wa Nsomba.

2. Ma Pond liners amalimbana ndi zovuta zamadzi monga kusefukira, kusowa kwa madzi komanso kusintha kwa nyengo.

3. Njirayi imapatsa mphamvu alimi a nsomba kuti azitha kuyang'anira ntchito zawo mosavuta komaso, kukhala ndi malo otetezeka ndi ofikilika.

4. Njirayi umpatsa alimi chisankho chosakha m’mene ma dziwe awa angaonekele koma ndi malo oyikapo.

5. Ukadaulo umapezeka mosavuta

Mukafuna kudziwa za mbiri Imbani kapena tiyakhuleni kudzela pa matsamba anthu a mchezo a WhatsApp kapena Facebook

Phone Calls: +265883075094
WhatsApp: +265883075094
Email: [email protected]
Facebook:
Location: Area 24, Lilongwe

Your trusted partner in fish farming and water storage solutions

16/08/2026

Backyard fish farming

Mukafuna kudziwa za mbiri Imbani kapena tiyakhuleni kudzela pa matsamba anthu a mchezo a WhatsApp kapena Facebook

Phone Calls: +265883075094
WhatsApp: +265883075094
Email: [email protected]
Facebook:
Location: Area 24, Lilongwe

Your trusted partner in fish farming and water storage solutions.

13/08/2026
ZINTHU ZISANU ZOFUNIKA KWAMBIRI PA ULIMI WA NSOMBAZinthu zisanu zofunika kwambiri pakuweta nsomba ndi izi: madzi okwanir...
11/08/2026

ZINTHU ZISANU ZOFUNIKA KWAMBIRI PA ULIMI WA NSOMBA

Zinthu zisanu zofunika kwambiri pakuweta nsomba ndi izi: madzi okwanira ndi abwino, malo abwino ndi dothi loyenera, msika ndi ogula, mtundu wa nsomba, komanso chakudya chabwino cha nsomba.

1. Madzi Okwanira ndi Abwino
2. Malo Abwino ndi Dothi Loyenera
3. Msika ndi Ogula
4. Mtundu wa Nsomba
5. Chakudya Chabwino cha Nsomba

Mukafuna kudziwa za mbiri Imbani kapena tiyakhuleni kudzela pa matsamba anthu a mchezo a WhatsApp kapena Facebook

Phone Calls: +265883075094
WhatsApp: +265883075094
Email: [email protected]
Facebook:
Location: Area 24, Lilongwe

Your trusted partner in fish farming and water storage solutions.

KUPHATIKIZA ULIMI WA NSOMBA NDI MA ULIMI ENA (FISH INTEGRATION)Kusakaniza ulimi wa nsomba ndi mitundu ina ya ulimi monga...
05/08/2026

KUPHATIKIZA ULIMI WA NSOMBA NDI MA ULIMI ENA (FISH INTEGRATION)

Kusakaniza ulimi wa nsomba ndi mitundu ina ya ulimi monga ziweto, ndiwo zamasamba, mpunga ndi zina ndi ndondomeko yabwino komaso yopindulitsa. Izi zimathandiza pakupanga chuma chochuluka ndi kagwiritsidwe ntchito ka bwino ka Malo.

N**i zitsanzo zausakaniza ulimi wa Nsomba ndi ma ulimi ena:

1. Nsomba pamodzi ndi mbalame (Nkhuku ndi khanga)

2. Nsomba pamodzi ndi ndiwo zamasamba (tomato, spinach, ndi zina).

3. Nsomba pamodzi ndi mbuzi kapena ng'ombe.

4. Nsomba pamodzi ndi nkhumba.

5. Nsomba pamodzi ndi mpunga

UBWINO WA KUSAKANIZA

1. Kugwiritsa ntchito bwino Malo.

2. Ndalama zochepa zogwiritsira ntchito.

3. Ndalama zimalowa nthawi zonse.

4. Kugwiritsa ntchito zinthu zomwe zilipo kale (raw materials)

Mukafuna kudziwa za mbiri Imbani kapena tiyakhuleni kudzela pa matsamba anthu a mchezo a WhatsApp kapena Facebook

Phone Calls: +265883075094
WhatsApp: +265883075094
Email: [email protected]
Facebook:
Location: Area 24, Lilongwe.

Your trusted partner in fish farming and water storage solutions.

KUOPSA KWA NYENGO YA El NIÑO PA ULIMI WA NSOMBANyengo ya El NIÑO imaika pa chiopsezo ma Ulimi ambiri kuphatikizapo Ulimi...
02/08/2026

KUOPSA KWA NYENGO YA El NIÑO PA ULIMI WA NSOMBA

Nyengo ya El NIÑO imaika pa chiopsezo ma Ulimi ambiri kuphatikizapo Ulimi wa Nsomba izi zimachitika kudzela pa kusowa kwa madzi, kutentha kwambiri kwa madzi, ndi kuchepa kwa chakudya. Zinthu izi zimachepetsa kukula kwa nsomba ngati chambo ndipo zimapangitsa kuti Nsomba zife.

1.Zovuta za Madzi ndi Kuchepa kwa madzi

1. Nyengo yowuma yaitali imachepetsa madzi m'mitsinje ndi pansi panthaka.

2.Kuuma kwa Madziwe

1. Chifukwa cha kusowa Ndi kutsika Kwa mulingo wa Madzi muthaka ma dziwe a nsomba amauma, ndipo ntchito yiweta Nsomba imakhala pa chiophyezo.

3.Kuunjizika kwa zinyalala Ma dziwe

1. Izi zimachepetsa Madzi zotsatila zake Madzi amaonongeka komaso Mpweya umachepa Madzi. chepa amachititsa kuti madzi.

4.Kutentha ndi Kuchepa kwa Chakudya

1.Kutentha kwambiri : Madzi otentha amachepetsa mpweya ndipo amapweteka nsomba.

2. Kusowa kwa chakudya: Chilala chimawononga mbewu za chimanga, n'kuyambitsa kukwera mtengo kwa chakudya cha nsomba.

5.Kukula pang'onopang'ono Kwa Nsomba

1. Chifukwa cha kusowa Kwa Mpweya Ndi Kutentha kwambiri Nsomba zimadya pang'ono ndipo zimakula pang'ono Ndi mochedwa.

6.Kukolola msanga:

1. Izi nditheka pamene mulimi akuika ukadaulo Ndi luso pa ulimi wake wa Nsomba pa Kasamalidwe, Machitidwe Ndi kapangidwe ka ulimi.

NJIRA ZOPEZELA MADZI

1. Alimi ayenera kutunga madzi a pansi panthaka: kugwiritsa ntchito Mijigo.

2. Kusunga madzi: Kukumba madziwe akuya ndi kuika mthunzi kumathandiza kuchepetsa kutuluka kwa madzi.

Mukafuna kudziwa za mbiri Imbani kapena tiyakhuleni kudzela pa matsamba anthu a mchezo a WhatsApp kapena Facebook

Phone Calls: +265883075094
WhatsApp: +265883075094
Email: [email protected]
Facebook:
Location: Area 24, Lilongwe.

Your trusted partner in fish farming and water storage solutions.

Address

Area 24
Lilongwe

Opening Hours

Monday 07:00 - 17:00
Tuesday 07:00 - 17:00
Wednesday 07:00 - 17:00
Thursday 07:00 - 17:00
Friday 07:00 - 12:00
Sunday 07:00 - 17:00

Telephone

+265888699966

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Newstart Aquaculture posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Newstart Aquaculture:

Shortcuts

Share