Tobias Ngozo Mr

Tobias Ngozo Mr Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Tobias Ngozo Mr, Business service, Area 47/4, Lilongwe.

Kodi munthu ukamwalira za 4n yako zimakhala bwanjiii
08/11/2025

Kodi munthu ukamwalira za 4n yako zimakhala bwanjiii

There is zero peace in leaving as a migrantSimeon Tobbie Ngozo
06/11/2025

There is zero peace in leaving as a migrant

Simeon Tobbie Ngozo

Mukazapita ku UK, Canada,USA, Israel, German, komanso ku South Africa ndipamene muzazindikire kuti abale anthu omwe ali kunja amatithandiza chifukwa cha Chikondi komanso Sacrifice osati kuti moyo wawo uli pabwino kapena ali nazo zochuluka👏🏻👏🏻👏🏻.

Kunjaku anthu ena ali ndi ma stress, they are depressed and kugwira ntchito akudwala because of us🫢.

Abale anthu akutukwanidwa daily, kusala tulo kuthamangitsa Dollar (ma shift) , kuzemba mbava, kulandidwa ma phone (Maka ku Joni) , ali ndi ziphyera zoti akaziona okha kumalira koma sangabwere kumudzi kuno akaganizira maudindo awo. Koma chikumbumtima cha kumudzi kuno amakhala nacho ndithu, they miss home, they miss their Children, they miss their husbands and Wives and they miss their Families😭

Mukazayenda ndikukhalako maiko akunjawa, Ka Mtendere ka muumphawika ka ku Malawi ka muzasiya kukaphweketsa🏃‍♂️🏃‍♂️🏃‍♂️

04/11/2025

Type B Charger ndiyontchajira ma Speaker guys 😂😂😂

Kodi mtedza mkam'phika ungamele??Simeon Tobbie Ngozo
01/11/2025

Kodi mtedza mkam'phika ungamele??

Simeon Tobbie Ngozo

Don't feel bad if you upload a picture and nobody comments on it. Who knows? maybe you left everyone speechless.Simeon T...
01/11/2025

Don't feel bad if you upload a picture and nobody comments on it. Who knows? maybe you left everyone speechless.
Simeon Tobbie Ngozo

27/08/2025
23/08/2025

Amunafe mmutu mwathu m'maenda zinthu zambri that's why timafika poiwala kuti tilindi mkazi kale 😄 mkufunsiranso wina😄😂😄😂

Akometsi
16/07/2025

Akometsi

05/07/2025

Kupita kukapeleka malowolo kumpoto ,popempha kuchotseledwa mtengo amalume amkazi amvekere achimwene musanenelere choncho mwanayutu ngokoma uyu mukamvanso inuo tapelekani zokwanilazo😂


゚viralシfypシ゚viralシalシ

Address

Area 47/4
Lilongwe

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Tobias Ngozo Mr posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share