13/10/2021
Ntchito Zikusowa I know that and malipilo amuzintchito zosiyanasiyana akukhala osakwanilitsa zosowa zathu and maluzi akupweteka pena kumayesa ngati ndiminyama from makolo koma funso kumati njira zina tikutsata kuti tithane ndimaluziwa ndi njira zanji nanga zomwe tayeselapo ndiziti nanga zomwe zakanika ndiziti,
Osaiwala zoti anthufe tikukula and lilipo tsiku matupi athuwa adzagonja adzafika pokanika kugwila ntchito chifukwa chakukula, kodi munaganzilako zatsogolo la ana anu omwe akubadwawo kuti adzakhala nditsogolo lotani ngati ife makolo tisakuchita kanthu kena kake tikadali ndimpamvu lero,
Ana akale ndi apano ndi osiyana kwambiri chifukwa nyengo zikusintha tsiku ndi tsiku nde mukuganiza kuti anawa angazaziphunzitse okha ngati ife tikukanika kuwapangila tsogololo lero,
Funso kodi munamvako za network marketing business or superlife chiyambileni??
Network marketing ndi industry yomwe ikugwilitsidwa ntchito ndima company ochuluka nziko lino , nde mwayi ulipo
Ngati mukufuna kuphunzira zambiri ndipezeni ku number iyi kuti muphunzire zambiri kuchokela kwa ineyo, pa +265881442132 ndipo mudzandithokoza bwino patsogolo mutaona kusintha.
Osandiweluzapo apa ngati zisakusangalatsa moyo wanu khalani chete kuweluza ndikwake Mulungu.