Chidwi

Chidwi Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Chidwi, Lilongwe.

28/05/2026

CAPE TOWN

is not safe , just watch ๐Ÿ˜ญ the video

๐Ÿ‡ฟ๐Ÿ‡ฆ๐Ÿ’”๐Ÿ•Š๏ธNKHANI YOMVETSA CHISONI โ€” Security officer wosalakwa waphedwa pa nthawi ya cash-in-transit robbery ku Moutsiya Mall...
28/05/2026

๐Ÿ‡ฟ๐Ÿ‡ฆ๐Ÿ’”๐Ÿ•Š๏ธNKHANI YOMVETSA CHISONI โ€” Security officer wosalakwa waphedwa pa nthawi ya cash-in-transit robbery ku Moutsiya Mall ndipo wasiya mwana wa miyezi itatu yokha.

โ—ฝMalingana ndi zomwe zatuluka, gulu la achifwamba okhala ndi mfuti zambiri linalowa mkati mwa mall ndikuwombera ma security officer pa nthawi yopereka ndalama kenako nkuthawa ndi ndalama zomwe kuchuluka kwake sikunadziwike. Munthuyu amadziwika kuti anali munthu wogwira ntchito molimbika komanso wosamalira banja lake.

May his soul rest in peace ๐Ÿ•Š๏ธ

Ife ndife akaswiri posaka nkhani ndipo inuyo simuzakhumudwa

Chidwi๐Ÿ–Š๏ธ๐Ÿ˜Ž

28-05-2026

THE ONLY NEWS YOU CAN TRUST
๐Ÿ‡ฒ๐Ÿ‡ผ๐Ÿ‡ฒ๐Ÿ‡ผ๐Ÿ‡ฒ๐Ÿ‡ผ๐Ÿ‡ฒ๐Ÿ‡ผ๐Ÿ‡ฒ๐Ÿ‡ผ๐Ÿ‡ฒ๐Ÿ‡ผ๐Ÿ‡ฒ๐Ÿ‡ผ๐Ÿ‡ฒ๐Ÿ‡ผ๐Ÿ‡ฒ๐Ÿ‡ผ๐Ÿ‡ฒ๐Ÿ‡ผ๐Ÿ‡ฒ๐Ÿ‡ผ๐Ÿ‡ฒ๐Ÿ‡ผ

25,500k Lilongwe area 23
27/05/2026

25,500k

Lilongwe area 23

MANKHWALA A DZINO A CHIKUDA.1. PEZANI MASAMBA A MASUKU A MTCHIRE A KU NSONGA2. WIRITSANI MASAMBAWO MPAKA ABWATE KOMA MUS...
25/05/2026

MANKHWALA A DZINO A CHIKUDA.
1. PEZANI MASAMBA A MASUKU A MTCHIRE A KU NSONGA
2. WIRITSANI MASAMBAWO MPAKA ABWATE KOMA MUSATHIREMO MCHERE
3. DIKIRANI APOLE
4. YAMBANI KUCHUKUCHA KU MBALI YOMWE DZINO LIKUPWETEKA
5. PANGANI ZIMENEZI MAMAWA, MASANA NDI MADZURO KWA MASIKU AWIRI BASI
6. DZINO LANU SILIDZAPWETEKANSO KUCHIRA KWANU NDI KOMWEKO

MITUNDU YA AKAZI OWAVALIRA CONDOMโ–ถ1. Okhala ndi tatoo๐Ÿ˜‚๐Ÿ™Œ2. Omwa mowa - mvalire condom๐Ÿ˜‚3. Ozimitsa foni akabwera kwanu๐Ÿ˜‚4. ...
13/05/2026

MITUNDU YA AKAZI OWAVALIRA CONDOMโ–ถ

1. Okhala ndi tatoo๐Ÿ˜‚๐Ÿ™Œ

2. Omwa mowa - mvalire condom๐Ÿ˜‚

3. Ozimitsa foni akabwera kwanu๐Ÿ˜‚

4. Aja amakuvula okha malaya๐Ÿ˜‚

5. Ngati adatinta tsitsi ,.. condom๐Ÿ˜‚

6. Ovala mikanda ... Condom๐Ÿ˜‚

7. Aja osakukumbusa kuti uvale kondom ... Condom bro๐Ÿ˜‚

8. Okonda facebook . Condom man๐Ÿ˜‚

9. Ngati ali ndi makanda ntchembere mvalireni condom๐Ÿ˜‚

10. Ngat amakhala yekha valani condom๐Ÿ˜‚

11. Ngati sakusuntha kumamgwira valani kondom๐Ÿ˜‚

12. Ngati amagwira ntchito ku saluni. Tchenan condom๐Ÿ˜‚

13. Aja amati amuna onse ndi ofanana... Condom๐Ÿ˜‚

14. Ngati amavala katcheni mmwendo , condom asee

15. Okonda misonkhano yandale , condom๐Ÿ˜‚

15. Ngat amaphunzira ku MZUNI, POLY , CHANCO .. condom baba๐Ÿ˜‚

16. Ngati profile pic yake pa facebook imadutsa 200 likes , mvalireni condom๐Ÿ˜‚

17. Ngati adapangapo post kuti ,' Single and happy' or ' No make up no problem' condom๐Ÿ˜‚

18. Secretary, condom๐Ÿ˜‚

19. Agent wa Airtel money, use 2 condoms๐Ÿคฃ

20. amene analemba pa Facebook dzina lake kuika beib kumapeto ,vala 3 condom ๐Ÿ˜†

21. Ngati dzina lake ndi; Jessica, Natasha, Patricia, Beauty, Jasinta, Sophia, Rita, Pretty, Glory , Rose, Monica, Ireen, Patuma,magret,Linda, CONDOM๐Ÿ’”๐Ÿƒ

12/05/2026

Chikondi chili ngat ma pod's๐Ÿ˜ฃ umasilila akakhala ndiwina koma ukagula ndipomwe umadziwa kuti ndiwosafunikila kwen kwen๐Ÿคฃ๐Ÿคฃ๐Ÿ™†โ€โ™€๏ธ๐Ÿ”ฅ

12/05/2026

You will find your place in God.

12/05/2026

Nde kwabwera business yogulitsa umuna ๐Ÿ™Œ๐Ÿ™Œ๐Ÿ™Œ๐Ÿ™Œnde akupanga offer ma dollar I was offered to be ambassador ๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚ ndawauza kuti zaugalu , zausatana ine ayi โ€ฆ.. kunjaku kukuchitika usatana ma member ๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ™Œ๐Ÿ™Œ๐Ÿ™Œ๐Ÿ™Œ akuti salary 50k in rands pa mwezi ,,,, anthu tikuyesedwa ndi satana ๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚

by SPIE

Wakana 11.5 Milion kwacha ๐Ÿ˜ฒ SPIE PIX wakana ndalama zosachepera 11.5 million Ku company ina yomwe imapanga business yoto...
12/05/2026

Wakana 11.5 Milion kwacha ๐Ÿ˜ฒ

SPIE PIX wakana ndalama zosachepera 11.5 million Ku company ina yomwe imapanga business yotolere umun@ wazibambo inamufikira kuti akhale ambassador wotolera mkakawu Kwa anthu Ndipo anamulonjeza kuti adzimupatsa 50,000 Rand's

Koma Spie Pix wakana uku akufinya kolona

let's do business@
11/04/2026

let's do business

@

Address

Lilongwe

Telephone

+265997617550

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Chidwi posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Chidwi:

Share