Andy Farm

Directions

Andy Farm The home of local animals

🗣️CHIDZIWITSOZomwe timagulitsa zatha🗣️Pa 26 September tiphuzitsana momwe tingapewere, ndikabayidwe ka fowl pox viral dis...
20/09/2026

🗣️CHIDZIWITSO
Zomwe timagulitsa zatha
🗣️Pa 26 September tiphuzitsana momwe tingapewere, ndikabayidwe ka fowl pox viral disease koma ndizapanga through video nde kwa omwe mumaoner ma video anga this is you advantage.
Mafunso ndi zina tizizafunsana ku comment section
Happy farmers happy animals 😊😊

Turkey for saleBreeds - narragasett, rayal palm, bronze and pure whitePrice range - 28 thousands (15 in total ), 38 thou...
16/09/2026

Turkey for sale
Breeds - narragasett, rayal palm, bronze and pure white
Price range - 28 thousands (15 in total ), 38 thousands (10 in total) and 50 thousands (10 in total.)
Contact - +265881267589
Location - Mitundu Lilongwe after bunda college

14/09/2026
🗣️CHENJEZOZiweto zambewu sagura tchembere, Musazati sinakuuzen. STAY BLESSED 🙏💚
12/09/2026

🗣️CHENJEZO
Ziweto zambewu sagura tchembere, Musazati sinakuuzen. STAY BLESSED 🙏💚

Onetsetsani k*t nkhola mwa nkhukundembo ndimosamalidwa bwino k*ti mupewe matenda monga..... Histomoniasi, coccidiosis, f...
06/09/2026

Onetsetsani k*t nkhola mwa nkhukundembo ndimosamalidwa bwino k*ti mupewe matenda monga..... Histomoniasi, coccidiosis, fowl cholera, respiratory infections kungotchurako ochepa.

Pamene mbalame (nkhuku, nkhukundembo, abankha, nkanga ndi zina) zatuluka ndi ana onetsetsani k*t kamwana kalikonse kamwa...
30/08/2026

Pamene mbalame (nkhuku, nkhukundembo, abankha, nkanga ndi zina) zatuluka ndi ana onetsetsani k*t kamwana kalikonse kamwa madzi aukhondo musanayambe kuxipatsa zakudya (feed).

CHIDZIWITSOTayambaso kuweta Akalulu
28/08/2026

CHIDZIWITSO
Tayambaso kuweta Akalulu

Born 10Breeds - palm, bronze and pure white Turkeys Age - 2 weeks and 4 days old No mortality 🙏
27/08/2026

Born 10
Breeds - palm, bronze and pure white Turkeys
Age - 2 weeks and 4 days old
No mortality 🙏

Still counting my blessings 🙏
27/08/2026

Still counting my blessings 🙏

Address

Mlale Mission Hospital Box 74 Mitundu Lilongwe
Lilongwe

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Andy Farm posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share