Azimayi A Single 265

Azimayi A Single 265 Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Azimayi A Single 265, Business service, Lilongwe.

22/04/2023
Hello Malawi Finest Singles Pali mkazi wa zaka 32 ndimakhala ku Blantyre.  Ndili ndi mwana mmodzi and ndili pantchito (f...
02/03/2023

Hello Malawi Finest Singles
Pali mkazi wa zaka 32 ndimakhala ku Blantyre. Ndili ndi mwana mmodzi and ndili pantchito (financially stable) ndikufuna mamuna wa serious wa banja. Akhale mamuna yemwe ali ready kulowa banja, at least wamwana tizizalelera limodzi. Oyambira zaka 33 upwards. BTW my name is Beatrice

Whatsap 0992201273

Morning guys ,. Thu beautiful lady is looking for a serious relationship her name is shirah ,,she is a malawian amakhala...
27/02/2023

Morning guys ,. Thu beautiful lady is looking for a serious relationship her name is shirah ,,she is a malawian amakhala Ku cape town,,,she is working Ali ndi mwana mmodzi basi koma alibe mwamuna,,,she wants a serious man to settle down with ,,,,koma akhale osachepela dzaka 30 ...

0992201273 for more information

Am a women aged 33 ndili ndimwana mmodzi.,not working  ndimapanga business  ndikufuna mamuna waserious  ofuna banja .Ine...
16/02/2023

Am a women aged 33 ndili ndimwana mmodzi.
,not working ndimapanga business ndikufuna mamuna waserious ofuna banja .Ine ndimapezekera ku Lilongwe koma kwanthu mkukhotakota.
0992201273 inbox

Ndine bambo wazaka 40 pano ndili ku mzimba komwe ndikugwira ntchito ya boma.mkazi akhale woyambira zaka 30-38 yemwe kusu...
12/02/2023

Ndine bambo wazaka 40 pano ndili ku mzimba komwe ndikugwira ntchito ya boma.mkazi akhale woyambira zaka 30-38 yemwe kusukulu adapitako komanso akugwira ntchito ngati lawyer,teacher,nurse or soldier.wa ana awiri kutsikira pansi vuto palibe chifukwa ine ndili ndi mwana mmodzi.

Ama man aged 44 single and with three kids, my type of woman should be understanding church going low self esteem and bl...
12/02/2023

Ama man aged 44 single and with three kids, my type of woman should be understanding church going low self esteem and black beauty nice figure as well beauty inside and out side thanks

Hello Malawi Finest Singles Ndine mkazi wa zaka 30 ndimakhala ku Blantyre.  Ndili ndi mwana mmodzi and ndili pantchito (...
11/02/2023

Hello Malawi Finest Singles
Ndine mkazi wa zaka 30 ndimakhala ku Blantyre. Ndili ndi mwana mmodzi and ndili pantchito (financially stable) ndikufuna mamuna wa serious wa banja. Akhale mamuna yemwe ali ready kulowa banja, at least wamwana tizizalelera limodzi. Oyambira zaka 33 upwards. BTW my name is Tamika

Whatsap 0992201273

Inbox  for more informationHello mummyIne Leah waku lilongwe ndufuna mamuna wa serous wabanja ndili ndi zaka 21 ndilibe ...
06/02/2023

Inbox for more information

Hello mummy
Ine Leah waku lilongwe ndufuna mamuna wa serous wabanja ndili ndi zaka 21 ndilibe mwana panopa ndikungokhala Kaye koma ndili ndi msce. Mamuna ayambire 26 wa serous osati time waster ai.

Aka ndika black natural beauty only serous guys

Address

Lilongwe

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Azimayi A Single 265 posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share