Alangizi265

Alangizi265 Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Alangizi265, Business service, Lilongwe.

13/03/2025

Ntchito ndi ntchito🔥

13/03/2025

Dzukani mukasake ndalama😂

13/03/2025
18/02/2025

🤝🤲

18/02/2025

My brother was to serious😂

06/02/2025

Naye tomato🍅 kudhula kuposa ndiwo ?😭

Kuzisaka kuzisaka kuzisaka!Kutipula kutipula kutipula!Kulimbikira monga mamuna mkofunikaKupanga ndalama mkofunika ndithu
31/01/2025

Kuzisaka kuzisaka kuzisaka!

Kutipula kutipula kutipula!

Kulimbikira monga mamuna mkofunika

Kupanga ndalama mkofunika ndithu

31/01/2025

Sadzakukwatirani ngati mapezedwe anu a chuma ndosakhazikika.

Adzakusiyani nthawi imene waona kuti mavuto azachuma akuchulukira.

Izi zikusonyesa kuti mamuna sakuyenera kungokhara ndi chuma chokhazikika chabe mkazi asanakhale naye serious,koma aonetsetseso kuti

•Asakumane ndi mavuto aza chuma
•Asakhale opanda kanthu
•Asataye ntchito yake

Kupanda apo adzakusiyani nthawi iliyose chifukwa cha aliyese wakuthekera yemwe ali pafupi.

Koma chosecho ndi atsikana omwewa omwe chiwelengero cha amuna omwe akhara nawo ndichoposa zaka za bambo awo kufuna Inu mukhazikike nawo posatengera kuti sakufuna kukhara ndi mamuna opanda kanthu.

Ngati sakufuna kukhara pomwe pali zochepa,inuyo mwaipa chani kuti mukhale pali zoipa ?

Boiz,tiyeni ngini tiionere patali.

Don't forget to follow

18/01/2025

Happiness is free😂😂

Address

Lilongwe

Telephone

+265991126110

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Alangizi265 posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share