21/05/2024
Talandiranso K100,000 ina akuti week ya mtondo yo tidzagawirenso anthu 20 ma K5,000.
Bwana awa amakhala ku America ndipo akuti daily salephera kuwona mmene tikuchezera pa page pano ndipo ati zimawachotsa nkhawa maka maka mukamang'alura zinthu zopusa. Iwo ati amadana zopusa ndipo amakondwa mukamang'alura.
Apapa ndiye kuti for 3 weeks we are safe. Pali K300,000 ndithu yoti tizigawa K100,000 every Sunday kwama Top Engagers. You become a top engager by commenting, sharing, watching videos and opening links on this page.
On a lighter note, ndiye kuti ndalama zizingokhala zopita kwama Top Engagers? Nanga Admin yo bwanji? Nayenso amavutika kusaka content. Chonde mabwana, mukamaganizira ma Top Engagers, muganizirekonso Admin. Zikomo.