Anointed pastor ken.

Directions

Anointed pastor ken. Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Anointed pastor ken., In-Home Service, Lilongwe.

21/09/2026

Yeremiya 29
11 Pakuti Ine ndikudziwa zimene ndinakukonzerani,” akutero Yehova, “ndimalingalira zabwino zokhazokha za inu osati zoyipa, ayi. Ndimalingalira zinthu zokupatsani chiyembekezo chenicheni pa za mʼtsogolo.

12 Nthawi imeneyo mudzandiyitana, ndi kunditama mopemba ndipo ndidzakumverani.

13 Mudzandifunafuna ndipo mudzandipeza. Mukadzandifuna ndi mtima wanu wonse

14 mudzandipezadi,” akutero Yehova, “ndipo ndidzakubwezerani zabwino zanu. Ndidzakusonkhanitsani kuchokera ku mayiko onse ndi kumalo konse kumene munali,” akutero Yehova, “ndipo ndidzakubweretsani kumalo kumene munali ndisanakuchotseni kukupititsani ku ukapolo.”

21/09/2026

Afilipi 1
6 Sindikukayika konse kuti Iye amene anayamba ntchito yabwino mwa inu adzayipitiriza ndi kuyimaliza mpaka pa tsiku la kubweranso kwa Khristu Yesu.

16/09/2026

Apolisi ku Ntchisi ati amanga anthu awiri powaganizira kuti apezeka ndi njinga yamoto ya mtundu wa King Lion yomwe akuyiganizira kuti ndiyakuba.

Mneneri wa polisi ya Ntchisi Salomy Zgambo wati anthuwa ndi Luka Baloyi wazaka 22 wamudzi mwa Kajumi ndi Ezron Banda wamudzi mwa James Zimba onse adera la mfumu yaikulu Mwabulambo m'boma la Mzimba.

Iye wati apolisi anatsinidwa khutu kuti oganizilidwawa achokera ku Mzimba kubwera m'mudzi mwa Chinsasa m'bomali kuti agulitse njingayi zomwe wati anthu derali anali kuwakayikira anthuwa pamomwe amatsetsira njingayi.

"Kutsatira izi ife ngati apolisi tinayamba kafukufuku wathu zomwe pakali pano takwanitsa kumanga anthuwa pomwe kwinaku tikusaka mwini njingayi." Watero Zgambo

Zgambo apa wayamikila anthu omwe akumatsina khutu apolisiwa pankhani zosiyanasiyana zawupandu ponena kuti izi zikuthandiza kukhwimitsa chitetezo m'madera.

Wolemba: Philord Kamagunda Magalasi

16/09/2026

Shout out to my newest followers! Excited to have you onboard! Yamzy Dada Kasambeni, Rowland Lingstone Chiwamboh, Aebu Chidanitsa, Kumbukani Kamtepa, Diffat Mtegha Mtegha, Tanazio Mwansambo, Enerst Poizon, Maah Mangilani, William Baloyi, Israel Christopher, Ag Beib, Pachalo Longw, Yami Bandah, Dairema Tchuwa, Emily Chiwalo, Young Jay, Dyvas Kondwani

phase 1
28/03/2026

phase 1

at the mountain for prayer and fasting
25/03/2026

at the mountain for prayer and fasting

Address

Lilongwe

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Anointed pastor ken. posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share