Uncle Soya Pieces Technologies Shop

Uncle Soya Pieces Technologies Shop Employment

Have ur choice today with uncle soya pieces computers shop
29/06/2022

Have ur choice today with uncle soya pieces computers shop

01/02/2022

Laptoos ,ma HDD ndi zina zambiri are available with us

28/01/2022

Azanu ayamba kale kuphunzira computer inu mukuti bwanji

16/01/2022

Have your good laptops & phonea at fair price we with us today
We also offer computer knowledge to every Malawian pa mtengo wosaboola mthumba
K*t muziwe zambiri tipezeni ku Lilongwe, Mitundu along cider load after Kadzakuwani shop kapena imbani phone
Pa +265 993 228 616/+265 884 536 379
Uncle Soya Pieces Computer's Shop! U name it, we print it!!!!

23/11/2021

azanu aja ayamba kuzatayisa nawo nthawi kuphunzila computer kuno inu mukudikira zichan?

13/11/2021
Kwa anthu nonse ozungulira dera la Mitundu ndi madera eni, tikukuziwisani kuti ife a Uncle Soya Pieces Computers timapan...
26/10/2021

Kwa anthu nonse ozungulira dera la Mitundu ndi madera eni, tikukuziwisani kuti ife a Uncle Soya Pieces Computers timapanga zinthu monga izi: Printing, photocopy, scaning, designing, Binding ife sitinathere p***a ai timapangaso zina monga: kukonza ma phone,radio,tv,dvd, kugulisa ma phone accessories monga lcd,touch,pocher,batteries,glass protectors, ndi zina zambiri pa mtengo wasabola mthumba, bwerani nonseeeee kuti mupeze thandizo lanu musavuta kapena imbani phone pa +265 993 228 616

19/10/2021

Halle guys, mwazuka bwanji lero

13/09/2020

SAMSUNG GALAX 32 GB going at 34 kuchoselana kulipo
Hit me on 0 992 838 937

25/08/2020

Paja mumafuna ka DVD ka boh kalipo
M***a kuika adapter, crash ndiso cd ndipezeni pa or call on 0 992 828 937

Address

Lilongwe

Telephone

+265993228616

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Uncle Soya Pieces Technologies Shop posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share