Thaik lon Painnkiller

Thaik lon Painnkiller Let us be radiant and shining
Never give up fi de lyfe 👏

03/03/2024

Uhure si chitaun mwava sister
🤏😎đŸĨēâ˜šī¸

Sweet news Edited by Thaik lon PainkillerPart one đŸ”Ĩ   "Mebo uli ndi figure yaboo  yoyenera kuifira,adatero Ras Vegas aku...
22/02/2024

Sweet news
Edited by Thaik lon Painkiller

Part one đŸ”Ĩ

"Mebo uli ndi figure yaboo yoyenera kuifira,adatero Ras Vegas akufusira"

"Choka apa uzikauza sister wako, adatero Meboo uku akuthamanga kumupewa Ras Vegas "

Nkhani yonse ili motere
👇👇👇👇👇👇
Ras Vegas anali ndi nzake Ras moze pamene amadya g***a pa hot spot yomwe inali mbali mwa manda,,,,kunena zoona inali spot yaboo mix chinthuzi cha mtengo wa Mango

Ali nkati mosuta adawona kankazi katali mwa size,koyerera, mahip aboo katavala chitenje koma nkatimo zimaonetsa kuti sadavale kathu coz chitenje chidazuzika ndi gwedegwede moti Ras Vegas adaivaira beib yo km maso ali psuuu red red ndi chamba.

Vegas: bobo, dzina lako ndani umakhala kuti, ukuoneka bwinotu

Nkazi:achimwene sindimacheza ndi anthu osuta chamba

Vg:man,,,sindidya zaza Pat,,iweyo tangokhala srs pat,l love you

Nkazi:nanga masowo red red mwa mesa unali pa hot spot iwe,ndimapadziwatu pa spot ineyo anyamata akuno ambiri amadya zaza amandibowa,okay?

Vegas:pakati pa zaza ndi ineyo akufusira ndani,,,heee? Tangoganiza,mmudzi muno uli ndi chibwezi? Ngati ulibe thako losero muzitani nalo nokhanokha 😏

Nkazi:😃😃😃😃,,,koma amuna enanu,,,,,, fundo zake zimenezo,,,,,,sudasambeso or phone ulibe

Vegas: za phone zo nde usakambe ndiri ndi necno spark 8c km ili pa charge,,,kusamba ndimasamba Friday ndi Sunday poti ndilibe beib km ndi iweyo ndizisamba daily kanayi pati

Ras Vegas adagwiradi nkaziyo poti adawonetsa ka life kodzichepetsa komanso nthabwara km za timing coz samaluza target kotero adapatsana hug and kiss 😘 adasiyana aras pa lisani patavutiratu muziwa Ras kukhalisa asadaonepo nkazi live mix ,,,, Vegas adali okondwa kwambiri chifukwa nkaziyu anali self container zonse mmomo....adagwirizana zoti macheza apitirira pa phone

Next part,,,,two
Tiyeni tiwone kuti zikhala zotani mmu part two coz amamufuna ndi ambiri moti aras alimbe nazo eeeeee

Just like en share this story to bring more vibes đŸ”Ĩ🙏

07/02/2024

Ndilibe dollar that's why ndikuzisaka
Apa ndikuvaya zambia lusaka
kumalawi ndatopa kugulitsa masaka
đŸ¤đŸ˜ŽđŸ•¯ī¸đŸ”ĨđŸ”ĨđŸ”Ĩâ€ŧī¸

04/02/2024

Some people are just sharing their problems rather than finding solutions to combat issues so that's why they still under combustion
....🙄🤏😎

01/02/2024

Life just needs a money
other wise you 'll be depressed with others 🤏😎

Abwinodi sakhalitsa ndatha kuona mmmmm Malawi sali safe      Good journey our artist          😭😭😭😭😭😭
08/10/2023

Abwinodi sakhalitsa ndatha kuona mmmmm Malawi sali safe
Good journey our artist
😭😭😭😭😭😭

Address

Kasipa 45
Lilongwe

Telephone

+265990876839

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Thaik lon Painnkiller posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share